Email a copy of 'Vote recount bid lacks merit, court rejects DPP’s Mussa' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Vote recount bid lacks merit, court rejects DPP’s Mussa' to a friend
After suffering two consecutive defeats in the ongoing TNM Super League, Moyale Barracks and Blue Eagles got back to their...
zitsiru izo kupanda manyazi ati,msiyeni mai zomba central nyake kuzolowera kuba vianthu va dpp kuba, niyo yaku 23 akuti bantile kaya sadawine iii koma Ivy palibenso dziko likanati liri nama jaji atoto moyo bwezi lili lokoma koma a vima jaji vina dyera inu simukalowa kumwamba mulapiletu msanafe ndi okupasani vindalama nonse lapani musanafe
Mufa muwona zitsiru mshiiiii…….adpp PAKUTI PANU NDIKUTI NONSE, kuyambira kaigwe kanuko shupit ZANA ASATANA INU.
Al shabab tamangovayani komanso mwina parliament ikukanani simuli mgulu logula nyumba za MHC mokuba inu go to hell.We don’t want ambassadors like you shupit
Once beaten twice shy. A DPP mukuti chani pamenepa. Mwangoti ziii ngati akuthirani madzi a mu fridge.
Bwana Peter please send this Al kaida Yunusu to Afghanstan to work there. asatibowe ife.
a diphiphi inu mwakhala mukuwotcha ma warehouse anzanu akanena zoti tiwerengenso so whats so special with this al shabab jihadist called yunus mussa???????????? tongonyamukani muzipita kwa majihadist anzanu ku egypty komwe wakutumizani mathanyulayo muzikaphulitsana mabomba nokhanokha aluya!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
Koma Necton Mhura amawinako milandu? What does he teach his student? Mbola yeniyeni
Is he not lawyer wa tressa namathanga?
che yunusu kapitani akutumani pitsala wakubisani umanyazi akutumimizani kwa mtundu ofanana ndikhungu lanu kuno anthu akuda akutozani kwabasi
bambo Mussawa atopa ndi umphawi mavote onse munaotcha ndiye mavote ofuna kuwerengansowo mukapezera kuti. Mussa bvomerani kulephera kwanu mpando umenewu ndi wosiirana mwamva kodi?.