Email a copy of 'Wanderers 1- 1 Dwangwa United: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

9 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
ndondwa
ndondwa
7 years ago

Team Dwangwa amayerekedwa a noma atapambana ndi nyau za ku Lilongwe bola ine tinu yanga inapanga draw ndi Moyale koma nanga mpaka Dwangwa makanda eni eni manyazi bwaaaaa!

Chitani Tobias
7 years ago

Inu mumadana ndi Scova a good referee. Have you undergone training ya U referee inu? Simumadziwa malamulo. Pali zinthu zimene zimakhoza kulepheretsa zinthu za clear kukhala zalephereka. Pamakhala ntchitotu. Munthu umaona cholakwika and then decision. Ukamadana ndi mphunzitsi sudzakhoza subject yake ngakhale mayeso akaphweka zedi.

jj
jj
7 years ago

Neba kuwina pa silver ine kudabwa? Silver is punch bag for th year. Tiye nazo neba. Kkkkk

race Rashie
race Rashie
7 years ago

Chaka chino kukhara mpira okoma mapeto ndutha kuona team ina yaikulu ikutuluka leage..its 2 early to pridct this koma ineo ndaziona kare zimenezi sungani mawu anga..

EDWARD NYONGO
EDWARD NYONGO
7 years ago

musanamizile referee koma simutha mpira,kudrawer ndi ana.

Tomoka John
Tomoka John
7 years ago

lnu zoti Scova amasapota Bullets simuziwa anali ndi sanje .mbuzi yimeneyo yisazayimbireso game ya Wanderers. Komaso aCoach munaganiza bwanji kupha Mawing’a mpira osasewerera kuyeserera

bambo wa Bushi ndi Dingi
bambo wa Bushi ndi Dingi
7 years ago

Neba umuuze frasisco sikova ndi omuthandizira wakeyo kuti izi sindale akamaimbira mwa uchitsiru chomwechi sizimuthandiza.Kodi Noma idzisewera ndi anthu angati? Iwenso tewesa usiye kugula ma ref. Tazidziwa ufufuzidwa.Zimenezi udayamba kalekale zik
akhala ndale zidakukani.Tindale takoto topusato nditimene timakupusitsani kuti mudziona ngati muchita bwino mapeto ake fomboni yeniyeni nkumakukanikani. Uchitsiru, sudziwanso kuti uchita utsiru.

Davie man
Davie man
7 years ago

Neba umati utani lero zagwa painu matama anthu inu last week munayankhula kunya agalu inu bullets ita drawer ndi Moyale pompo. Pajatu mumati mwayamba bwino lero ndi izi. Linda madzi apite kenako uziti wadala. Inu nde manyaka basi!!

Mphatso
7 years ago

Big up to new comer(Dwangwa) 4 de work sprit u hve shown veteran team in TNM SUPER L,its possible 2 do well lets take example of international club(barclays)..Leicieter City

Read previous post:
Does Malawi have a post turtle for a president? I beg to differ

In this era of freedom, even the seemingly free individual is unfree; the general outlook being that of a liberated...

Close