Email a copy of 'Wanderers accuse FA Malawi of ‘double standards’ over Chande’s contract saga' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers accuse FA Malawi of ‘double standards’ over Chande’s contract saga' to a friend
The office of the United Nations Development Programme (UNDP) in Malawi has warned Malawians against bogus adverts circulating on various...
FAM, justice delayed is justice denied. When yu delay more confusions emerges
Wasuzgo bwanji? Musiyeni mwana inu!
Agaru a FAM mwakhomerela Dedza panonso mukufuna kukhomerele manoma, agaru!!
Ngati Chande anasayina contract ya one and half year, ndiye kuti mlanduwu ndi obvuta kwambiri. Ndipofunika kufatsa. Chande angatole thumba mtsogolomuno ndiiithu………..
Musaiwale kuti FAM ikulamulilidwa ndi agalu, Makamaka ameneyu otchedwa suzo Nyirendayu.
zikuvuta pati kungogamula.sizokha zokha za a Gomezani Zakazaka zomasintha zovala akapita ku game ya Bullets makamaka ikamawina.
akanakhala kuti player wachoka ku NOMA kupita ku Maule sakanavuta.
FAM pELEKANI UFULU KWA MA PLAYER MOMWE Boma linapelekera ufulu kwa ma Hule.
Kodi nkhani yake ndi itiiti ikuvuta kugamula apapayi,, mukumuphera tsogolo mfanayu pangani mwachangu ayambe kusewera kulikonse kumene atapiteko. Dziko ili anthu ake onse ndondoli basi mxiii!!
nyirenda nyooo
Apatu malamulo agwire tchito….apo biii ife timatcha. Some-1 here forged a document and some-1’s signature. Laws of Malawi where are you? This is serious offence!
Momuja Achita Resolve Lit?
Stupid Suzgo and his entire FAM. What do they exactly want or to do with innocent Chande. The one who signed the contract has authenticated that Chande submitted to FAM an original copy of the contract. What else do they want?? I wonder what capacity do these guys have at FAM. Suzgo and your friends, please, just resign if you cannot manage to deliver….. Period!!!!!!!