Number 4 ukunama tu iwe Nyerere ndi deal. Jersey yokongola ngati yimeyi wawona bwanji nebor mmene tikukunthila mafriendlys neigbor samala kwambiri ka tnm uko tingakulande ukapusa.
Guys tayamba kuvala jersey imeneyi? Anyway no problem zinthu zikusintha
Generation of vipers
8 years ago
Kodi ndi PP wanderers ?????
Desire Nyasa
8 years ago
Neba ukagulensotu ma player ku chilumba. Pajaiwe player akangogolesa chigoli ku training chosatila ndikumugula basi kkkkkkk what about Nakamura the mechanic is he adefender or goalkeeper ?????
crispin Gracious Fodya
8 years ago
Kkkkkk!!!!!!!kodi Nakamura ndi wampira?? Kapena mechanic wa Japanise used Cars idont see him scoring !!!!!neba wabesatu iweee
SAMSON WA NYELERE GANG'A CHINANGWA
8 years ago
Nyelere ndi nyelere basi chaka chokolora ndi cino kuli NYEE!!!!!…….!…………KULI NYE!!!!!…..LERE KU….>NOMA
kkkkk mablues amenewa kapena maOrange
koma ka blue kaja kamafunikabe
Number 4 ukunama tu iwe Nyerere ndi deal. Jersey yokongola ngati yimeyi wawona bwanji nebor mmene tikukunthila mafriendlys neigbor samala kwambiri ka tnm uko tingakulande ukapusa.
Jersey ndiyokongola abale i wish tizi user that color. Beautifull jersey guyz.