Email a copy of 'Wanderers sign striker Peter Wadabwa' to a friend * Required Field Your Name: * Your E-Mail: * Your Remark: Friend's Name: * Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries. Friend's E-Mail: * Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries. Image Verification: * Loading ... Sharing is caring! 0 shares Share Tweet Pin LinkedIn Email Print
kkkk mpaka wadabwa gutys
Nkhalamba
zuli bwino kwambiri
a Butao zomwe mwachita ndizokomela family ya kwanu osati mafanzfe ayi muzifunsila nzeru kwa D kanyenda momwe ankachitila mwatibowa ndi wadabwa wanuyo
big up wadabwa
welcome
Mpakana Wadabwa? Mmmmmmmmmm……..koma ife a Noma nde kayatu, sitizatheka. He’s a spent force!!!!! Silver ikamasiya munthu ndekuti chatha ntchito. A Madeya kaya timati Madeira, mwatani kodi?
Neba do u know how old z Sulumba , Lanjesi and Zoya ? ngati amenya Civo kwa zaka 8 ndy pano ali bwa ?
Zilibwino experience is a great teacher, watsala goakeeper chipuwa timulole apite.
zili bwino, keep it up.