Wanderers surrender on title chase, it’s for BB: Malawi TNM Super League

Mighty Be Forward Wanderers has effectively surrendered the TNM Super League title to their rivals  Big Bullets after their 1-0 defeat on Saturday at Kamuzu Stadium.

Time to surrende: Coach Elijah Kananji and technical director Yasin Osman -.Photo Jeromy Kadewere

Time to surrende: Coach Elijah Kananji and technical director Yasin Osman -.Photo Jeromy Kadewere

Heads down for the Nomads...Photo Jeromy Kadewere

Heads down for the Nomads…Photo Jeromy Kadewere

Nomads fans in disbelief...Photo Jeromy Kadewere

Nomads fans in disbelief…Photo Jeromy Kadewere

The Nomads are 15 points behind the Peoples Team and the club ‘steam manager Steve Madeira does not appear to hold out much hope of catching the leaders.

Bullets are currently basking comfortably on the summit table maintaining their unbeaten start to the campaign.

Madeira said the Nomads “have no chance” of winning the league, “we are not in it.”

“Look at the number of points they have today and if they keep that up nobody will touch them, that’s for sure,” said Madeira

“It doesn’t look like anybody is capable of challenging them at the moment. There’s no obvious reason, but they have had a good league campaign,” said Madeira.

Madeira conceded that they were outplayed by Bullets and saluted his goalkeeper Richard Chipuwa for saving the team to a big embarrassment.

“Congratulations to Bullets for their victory. They really outplayed us and we can a swell rule ourselves out of contention,” said Madeira.

He said they will now focus on the Standard Bank Knockout Cup.

Follow and Subscribe Nyasa TV :

Please share this Article if you like Email This Post Email This Post

More From the World

44 thoughts on “Wanderers surrender on title chase, it’s for BB: Malawi TNM Super League”

 1. Petersen shymam mandala says:

  Neba uzikalimbana ndi ana anzako omwe ali kumusiwa

 2. west bouy says:

  kuyankhula koma kumeneku

 3. Notis gogoda says:

  Usathe mau neba

 4. Grenard anderson says:

  Maule more fire aneba ndi ana abwerele ku ligi yaying’ono

 5. CHESILIKA says:

  maulleee kut wawawa MFL (Maulle For Life)

 6. CHESILIKA says:

  uziona neba maulle ali ready for any attack kkkk

 7. Pokelloe says:

  mukuona ngati muzawina inu

 8. Preciousmaulidibanda says:

  Nanenso ndkumatha kuona kut bb ikufnika FA CUP, znaz mhh ndzofnika kabwafu united

 9. Richard Manjatika says:

  Kuvomereza a wanderers kumawavuta.Bullets ndi team yodalitsidwa basi.Iwo amakhala ndi chilichonse koma mu mpira adapangako mbiri yanji yoti muno mu africa kuwadziwa? Mudakaphunzirabe mpira

 10. maule in mozambique. says:

  Ana achepa, ife size yanthu ndi Caf osati TNM League, awa ndi ma practices chabe!

 11. bambo says:

  Hw can real manager like madeira surrender the tittle with 11 games to play. I never seen bullshit manager in my whole life like him. Its too premature to say that’ mr manager.’ oky? If you don’t know football you better quit and give the room for other guys. Noma keep on fighting the league is not yet over. Nyerereeeeeeeeeeeeeeeeeeee woyyyyyyyyyyyyyyyyyy.

 12. Pampha la lichero says:

  Ana achepa awa akabadwe katatu

 13. humphreys says:

  League yatichepela iyi,ofunika tikamenye barclays,maule woyeeee!!!

 14. uli boo madeira koma dziwani kuti its ten years madakalira

 15. Captainmwanamwana says:

  Dzikomo kwambiri neba ,wawonetsa chitsanzo chabwino.

 16. MULHOMWE WANKULU says:

  Galu uyu Coach Elia Kananji angamanene kuti referee anatikanila Penalty, zopusa basi. Ife Anyerere matama too much kaya chifukwa poti tili ndika sponsorship kochokela kwa Aluyawa……Anzathu Amaule samanziva ayi kuyambila ma Player mpaka ma Sapota awo, koma ife ayi timvekele mfwemfwemfweeeeeee ndabetcha Galimoto yanga, Nyumba, Ndalama, Nkazi wanga ndizina zotere, zopusa basi. Choti tidziwe kuyambira lero ife Anyerere nchoti mpira sipakamwa ayi koma ndipa galaundi and its played for 90minutes, period!!!!!!! Apa nde tazionatu mbwaza. Elia ungolimbikila Std Bank Cup apo biiiiii tikuyatsila koloboyi ulendo wakwanu. Wopusa iwe kwambiri. Big up to our Team Mgr Steve Madeira for accepting that genuine defeat osati za Elia’zo.

 17. ZZ Junior says:

  There will always be problems at Manona. This is their own making. Look here wanderers has Medeira as team manager which is okay. Then they have this list, Yasin Osman as tech director, Ed Ngonamo as tech director, Elijah Kananji as Head Coach, Chiyembekezo Zidana as who so ever. All these four shout instruction from the bench during game time. I wonder who is in charge and who actually trains the team. We all know Yasin ndiwokula mtima bad. he cant take anything from Kananji. this has effectively confused the players. Remember too many cooks spoiled the brooth. Come on Butao, give young man Kananji the freedom he deserves. Borrow a leaf from Bullets.

 18. Mbewa zatha says:

  Tikamati u sportsmanship Mr. Madeira ndi umenewu, kumathokoza pamene pafunika kuthokoza. osaangolira chilungamo mukuchidzwiwa kuti BB ndi team ya mfuko

 19. phwethulani says:

  Maule ndi nyatwa wawa

 20. ella chimtengo says:

  zoona

 21. ELLA CHIMTENGO says:

  zikutheka!!

 22. njuli says:

  That’s being positive Mr Madeira giving credit where it is due osangodandaula zilizonse, ife tinalephera Carlesberg cup, tinavomereza just to avoid violence. Whether some nyerere fans like it or not the fact is BB ndi timu yokhanzikika without sponsors yet doing well on the ground, ndi membership titayambeyi, zolira lira will be a thing of the past, anyamata athu azisangalala, nawonso azimwa wamkaka asamangotimwetsa ma sapota tokhafe. Timangokumverani mukutokota masapota a noma yet ife a BB mau athu mpang’ono chabe, dikirani 90 mins, mpira wapakamwa ife tinasiya, can’t you borrow a leaf, kulankhula lankhula sibwino, mwamuna nzako mpachulu umalinga utakwerapo, dinda madzi apite ndipo uziti ndadala BB woyeeeeee!

 23. sub wa bullets says:

  WA mkaka maule

 24. imraan allan says:

  mkulu ameneyu wandisangalatsa kwabasi chilungamo wachiwona kuti BB zake zikuyenda jelous down

 25. Titus Skoti says:

  That is what we call kukhwima maganizo. a Madeira avomereza kuti momwe zithu ziririmu, it’s not possible to think of NOMADS getting the TNM Super League. Koma ena kumangodandaula za ma referee all the time.

 26. yazula says:

  A Madeira zikomo apa mwaonetsa chamuna ,kumavomereza osati za a Nkunika chimutu pwi pa TV ngati amadziwa mpira. Anatani iyeyo kukaimbira ngati amadziwa bwino mpirawo? Mwaona lero kuti goalkeeper amayenera kutetezedwa?Ubwino wake sindiwe ref komanso sudzakhalanso,kuzolowera kugula ma ref basi ,musovenge kkkkkkkkk hihihihihi hahahaha

 27. Victor says:

  Mr.Madeira,that is good for sports we have to accept and congratulate others when they are doing well.You are honest man.Lets learn from Madeira to develop the game of soccer envy doesn’t help.Bullets keep it up and Manoma just continue working hard it will work tomorrow.

 28. sapota says:

  bravo bullets!!

 29. Konyapapa Nyapani says:

  Paja Bullets ikayamba kutenga league kamakhala ka 7 motsogozetsa

 30. zeni_zeni says:

  I still love The Nomads

 31. Lovemaniac 91 says:

  Who is next to surrender? # feels gud to be back in love!

 32. Duncan kapunda says:

  That’s hw God has choosen ,let us drink wamkaka now

 33. patrick kamkwende says:

  akalenga ndinu wanthu, tengani naomi akhale wanu

 34. SUPPORTER says:

  Now here comes de PEOPLE’S TEAM Goloooooo!!!!!!!!!!!!!!

 35. ROBERTO says:

  Ife timaziwa kuti sangapite nazo patali,prepare for 2020 season my be

 36. Lure says:

  This is the bullets I know, watch the space, next season we are merging with FISD tiphuzitse anthu mpira

 37. REAL BULLETS FUN says:

  Madeira mwavomeleza ena samatha kuyamika zikomo a team manager

 38. Hardson says:

  Madeira! I think you are a good and intelligent administrator ever lived in this part of the world. Big up to you and wish you well as you are indeed concetrating on Standard Bank knock out cup. Bullets!!!! Legea yaonetsa kutsa kudengula komano cup tiye nayoni nafenso tione kusintha

 39. Ngakhale Kamuzu anavomeleza kulephera chisankho asanamalize kuwelenga nthawi imeneyo annthu ngati a Chakuamba asakumvesa kuti iyayi afike kaye ku mapeto kuti mwina zisintha!Manoma umenewo nde umuna kumavomeleza kumenyedwa ngakhale ena ku Be Forward ko sakuvomeleza!Nde pano ndikukupephani kuti nonse a noma munene mau awa; “Bullets woyeeeeee, Chande Woyeee,Ndipo mutenga Galimoto ya a NAYO!”

 40. BBpipos team says:

  Neba uku ndiye kuyankhula osati kumangolila.maule ndi akatakwe man.Mwina zikayenda tikugayira ka 10 points neba.Nanga neba adzivutika sibwinotuyi kukhala satero pamudzi.choncho neba masiku sakoma onse napepe.

 41. opportunist says:

  Ana achepa

 42. Ophiri says:

  Neba chimenecho ndicho chamuna,kumaimika manja zinthu zikavuta.Ndiye ngat akuimika manja a nyerere enanu ndiye kakaka,muziona.MAULLEEEE MOTO KUTI BUUUUUUUUUUUU!

 43. Thank Almighty God for helping Bullets to beat aka Nyerere.U really made us happy.

 44. Muzaza says:

  BULLETS WOYEEEEEEEE!

Comments are closed.

More From Nyasatimes