Email a copy of 'Water boards give Malawi govt 14 days for pay rise: Threaten to lock taps dry' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Water boards give Malawi govt 14 days for pay rise: Threaten to lock taps dry' to a friend
Mzuzu University (Mzuni) student Dumisani Kagunga Kaunga, accused of defrauding the university more than K2.2 million ($3 175)) in a mini...
Mukatseka madziwo kuti poti madziwo sakutuluka ndi kale agalu inu ntchito ikukulepherani apa kukweza malipiro achani? Ngati ndalama zikuchepa kayambeni gain yogula mbeu asiyileni ntchito amene aliokonzeka kutukula dzikoli musanyintirika …
Maziwo muzikaseka ku Area 10,11,12,47,3 komaso Namiwawa,Sunnyside,Mudi….ndikomwe zisiru zomwe zimakweza kopena kudya ndalama zaboma after atagwira ka ntchito kang’onong’ono….mwina kungokwera galimoto ndikukakhala guest of honor…koma dola yokhayo utha kupanga transport yopitira kumuzi ku chitipa mpaka kusala ndi chenji….muwasekele azitunga mazi kuofesi mbuzi zimenezi……ife tinazolowela kumwa amuzithapwi…….waganyu sadwala amadwala ndi mabwana
Madzi sakutuluka do u thing boma ndalama lizitenga kuti zokulipilani inu.
Mukanika ntchito komaso mukufuna kukolola posalima ngati ntchito simukutha just pack and go komaso boma could thing to abolish old sysyem of company registration. Likanaitana ma companies that are legible to offer good services for the better of Malawians rather than these mbuli. Good service good pay poor service poor pay.