Email a copy of 'Zodiak to host live FA Malawi presidential elections debate: Candidates to unveil manifestos' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Zodiak to host live FA Malawi presidential elections debate: Candidates to unveil manifestos' to a friend
Malawi’s leading choral grouping, Great Angels has resurfaced on the scene with a launch tour of music videos of its...
Yabwanya will be fam next presdent.good luck to u yabwanya
walter wawina kale izi…wina afune or asafune!
Nyamilandu nthawi yanu yatha chitani manyazi sepp style eti mwachita taona mulibe manyazi eti.
Mijiga , Mijiga more fire , enanu mwakhalapo pa mpando wu koma still no development asiyeni azanu ayesenso mwina mpira ungasintheko pa Malawi pano , please, please ,please chonde a Walter kkkkkkk.
Nyamilandu baasi!
CHONDE ULENDO UNO , PRESIDENT WA FAM VOICE YAKE IKALEKO YOMBVEKA BWINO OSATI NGATI ‘ RADIO ‘ YIKUTA MA BATTERIES
‘INENSO ‘ NDINE WAPAKAMWA BWANJI….
Walter ndi katundu
a Walter, having already served for 3 terms, what new do you think you can offer? corruption eti? Asiyeni anzanu ayese nawo. Mwachita mbali yanu molephera momwemo
kkkkkkkkkkk
Mijiga Mijiga mijiga,,,,,,ndi owinawina kale,,,,,,palibenanso cholesa,,,,,,,,Mijiga more fireeeeeee,,,,,am wishing him well
My man remains Chomanika. His vision for Malawi football is most impressive BUT the system set him aside. Regrettable!