Email a copy of 'Zomba shooting incident causes postponement of Civo, KB game' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Zomba shooting incident causes postponement of Civo, KB game' to a friend
A two-day national stakeholders forum organised by Public Affairs Committee (PAC) on inclusivity and federalism, aimed at enhancing common understanding...
silikali yo ndiworakwa chifukwa iye futiyo amafuna kutiataninayo
sanalakwe wa policeyo koma vuto asilikari akumalawi matama simuparemekeza ntchito ya mzanu
kulanda mfuti nde zoopsa. Amalanda kuti atani nayo mfutiyo?
wapolice sadalakwe. iye amagwira ntchito yake. vuto asirikali amayenda ndi ntchito pena paliponse. iye ngati munthu wozindikira zachitetezo apanga bwanji ganizo lolanda mufti wa police.
Due to rise of insecurity,the police was quite right 4 the interest of the nation and hz own dfence.these guyz(soldiers) hav no manners.he was supposed to b treated lyk any vacabonder.
let me tell MDF officers kuti ngati asilikali apolisi simukuwafuna auzeni kuti asiye kugwira ntchito muzigwira ndinuyo becoz pali asilikali a MDF ena mkhalidwe alibe amafuna azzasokoneza apolisi pathawi ya ntchito,palibe msilikali angalore kulanditsa mfuti sibwino zithu kupangira mphanvu now me as a malawian am saying auzeni asiye muzigwira ndinu
thats bushit why the police kill them
Sorry Sodiers, but your anger can prove a fresh bias. Do this against deaths of innocent people who are normally brutaly murdered, and use such action to frighten all murderers!
I love the USA Army, professionals ever.
The soldiers in malawi are arrogant and uneducated to an extent. they don’t know their roles in society and always feel supreme. The policeman did the right thing for it was self-defence to a drunkard citizen.