Email a copy of '10 year jail term for impregnating step daughter in Mzuzu' to a friend
Loading ...
Email a copy of '10 year jail term for impregnating step daughter in Mzuzu' to a friend
South Africa President Jacob Zuma Monday lashed out at Africa governments who “criticise the South African government but their citizens are...
Anthunu mukunena zoona. Ine ndinalowa gule ndipo nkatiphunzitsa kuchinda kokha basi. Ndiyr maresult ake ndiwa. If you voted for Chakwera, panopa dere odala tiana tikanaona ife agule wochewa eni-eni. Mutinjata panopa chifukwa poti boma lili mumanja wa Mulako
mudzikapanga kwanuko zimenezo vilombo inu, agalu inu, mutisiyire chigawo chathu chokongolachi iyaaaaaaaaaa!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
that’s child abuse,how can he do such a thing 2 an innocent dota.plz let us think b4 we act.
Ndizimene amakonda azanthu anyau zimenezo.Sukulu ndi mpongozi koma akati zigololo ndiye no 1.
Akamabwera azapeza mkazi wake atakalamba.
akasave koma zaka zachepa.
Munthu oipa kwabasi
Achitabwino
Ngakhale nkhuku zimamwa mazira awo kkkkkkk usova!!
Anthuwa akutiwonongera chigawo chathu, Tazipitani mukapangwe kwanuko bwanji kodi? izo zikuchitika lu Mchinji kupha munthu ngati nkhuku zoona?