Email a copy of 'Ministry of Health drivers plan to petition administrator over ill treatment' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
History Repeats
6 years ago

Allowance gate ndiyo yavuta apa. Its has always been a normal practice for officers to change their drivers whenever need be.

AAlex
AAlex
6 years ago

Atawapanga post kwina ma driver aku CHSU zingakhale bwino chifukwa anthuwa amayiwala kuti ndi ma driver a boma. Kukhala ngati anthuwa ndalama akumapeza zabwinoko and chifukwa ndima driver ka moyo ka usavage ali nako nkumamaziwonetsa ngati iwowo ndiye ma officer a ku CHSU. Ma driver anzawo a mmadepartment ena sawawona kanthu. Izi sizoyipa kupeza ndalama koma ntchito ya mboma munthu utha kupangidwa post kwina ndi mmene bwana owonela ma drver waganizila. Chifukwa choti ma officer ena amapanga chinyengo ndi ma driver ena pa nkhani zina monga mafuta ndi zina zokhuzana ndi ma galimoto safuna kulandila ma driver ena pa officepo.… Read more »

driver
driver
6 years ago
Reply to  AAlex

Hahaha vuto ndiloti anakumanani. Anamanga ma den. Ali ndi ma motor. Inu zanu mumathera kugula ma jumbo a mahule nde mukupanga nsanje. Are you aware that ma driver amapanga okha service, kugula matyre even fuel wa local running? Nde ukati ma driver akuononga chuma what do you mean?driver ukumusakayo amene ukuti savage yo, amavomereza umbuli nkona amalimbikila kuti akamadzapuma asadzakhale kapolo ngati iweyo omangothera pa rent. Shupit

Titi Fulu
Titi Fulu
6 years ago

This is a laughable article mostly likely to have been written by one of the driver’s relation. All drivers are ministry of Health employees and can be transferred anytime. These drivers were not employed by CHSU they are simply deployed there. Dyela lavutatu apa. Why shouldn’t others drivers benefit? If it was not for postings most of the drivers should never have been at CHSU. Let others also enjoy. All necessary procedures are followed in effecting postings and officer targeted here can only make recommendations. Mwangodana naye munthuyu. For your information PAO is US who is under DDA who is… Read more »

Ngalambe
Ngalambe
6 years ago

Just wondering, kodi a Adrian Chikumbe wa alibe photo ina? tawajambureni ina chonde kapena mupite pa FB mukatenge photo ina iyi yatikwana. Zikomo

observer
observer
6 years ago

you were fed with wrong info by the disgruntled drivers. mwati akukana internal posting nde administrator walakwa?
mwasakaniza nkhani zopanda ndi umboni kusonyeza mabodza eni eni

waloni
waloni
6 years ago

pali nkhani apa these drivers it seems are used to easy money allowances without going to the field vitsitsi has tightened the screws he wants aacountability and its normal in the civil service to transfer people nothing new

Awize
Awize
6 years ago
Reply to  waloni

These drivers are biting the finger that feeds them. Let them behave well. Govt employees can be transferred to any MDAs (Ministries, Departments and Agencies) when authorities deem it fit. Good for them to resign if they feel they are mis/ill-treadted and join Profit-oriented organizations, NGOs etc. That’s why Govt employees are known as “civil servants” (akapolo a boma) chifukwa servant mu Chichewa chomveka bwino ndi “kapolo”. Kapolo sakwiya. Case closed

Read previous post:
Malawians condemn disgusting football fans’ behaviour at Bingu Stadium

Malawians have strongly condemned and castigated disgusting behaviour of football fans who were captured urinating against the wall shying away...

Close