Email a copy of '2 interdicted for rape in Malawi health facilities: 26 for theft' to a friend
Loading ...
Email a copy of '2 interdicted for rape in Malawi health facilities: 26 for theft' to a friend
A new political party called the Union Party (UP) led by Canada-based former parliamentarian Paul Sydney Shawa is said to...
ku healthy kukubedwadi.opezeka ndi dismisal basi & akwagwire ukaidi.
The account at queens have been know to steal for along time, they get supplies, inflate prices and steal ask for commission 15%. They buy things not needed as long as they will get commission from drug and medical equipment vendors, especially those from their region. Its good those who steal are being dismissted and not transfered, there has been too much uchitsilu in district hopitals.
A meneo akapezeka kuti ndizoona amangadwe basi kuti azao atengelepo phuziro
WARNING: Health Surveillance Assistants are NOT healthcare workers; they never went to any medical sciences trainning college nor are they recruited on merit.They are therefore not licenced/trained to examine any patient!
ALIYENSE ADZAKOLORA ZOMWE WAFETSA.AMENEWA NDI AKAKOWA ODA M’MAGANIZO!!!!
koma ndiye wawona zowopsa
Wa 16yrs hw was she raped and was she pregnant sanamagidwe bwanji?
koma ndiye akufunika chilango chonkhwima kwambiri
aaaaa penapake boma likulakwisa paka namwino wa chimuna ku mudzi mukuona ngati atani? basitu iye kunyenya kanyenyayo.
Komanso mwamuiwala woba ma solar panel apacipatala ca kwa naombe ku phalombe ameneyu ndi medical assistant.