Email a copy of '45 children die from malnutrition: Malawi food shortage' to a friend
Loading ...
Email a copy of '45 children die from malnutrition: Malawi food shortage' to a friend
Ovy Network gearing itself to become the best TV beaming channel Operator in the SADC region will soon be operating...
A peter boma nde lakuvutanitu. kufa kwa ana awa magazzi awo alimmanja mwanu. apanso mwati sukulu anthu azilipira, jc std 8 wachotsa . apa nd mwatsegula makomo onse a mavuto mzdiko lino . muuti malata cement subsidy kodi anthu adya cementyo nde malatawo.
apatu mukutiuza kuti aziphunzira ndi anthu anan olemera,people are failing to pay k5000 ya ku community nde mwati k35 kaya k55 haaaa A peter mwataya mtundu wa a malawi. ndikuuzani ana ambiri sapita ku xul. ngati ndikunama muzandifune.
Mawu
In the same Country 300Million party for one day. 300 Million to give Mbendera for civic education. 100 people accompanying a president from a poor Country to US. Its ok for those kids to die as long as their business is as usual. Thank you all those on those positions. If you cannot speak for the oppressed God can use anything to bring the message across.
A Malawi mwayamba kuziwona ndi kuzigwira. Masankho anu ndi amenenwo. Peter Woyee. 2019 WO!! Mudzamusankhaso chifukwa cha dyele lanu. Anthu okanika inu. Njala ikukutumulani. Ndipo muva m’mbembe. Uku ndikuyamba chabe. Zambiri muziwonanga!
RIP inocent chidren
Dziko ndiwathu ndalama ndiwawo. Sitidaziimilebe patoka tipitirira kufa ainiwake akusakaza chuma ku UN
anthu andale nkhani ndikuba basi alibe mtima othandiza amw
Government please address this as in the 21st century this is not acceptable. Donors where are you we see you in papers telling do this do that its time take your moral responsibility and start helping poeple, Donors dont punish poor malawians for cashgate punish those who did.
Children are dying of malnutrition and our leaders are enjoying themselves (mapwevupwevu) in New York. Oh God deliver us from this evil. Our priorities are all upside down. Big and rich nations are sending very few delegates to this forum and poor Malawi thinks otherwise. We can afford to send over 100 delegates at the expense of these poor souls who are dying like flies….
Am i the only one here thinks that this nation should be put up for auction kkkkkk coz I don’t think adoption can be successful kkkkkk