Email a copy of 'Activist Kapito says demo does not make sense: Malawi CSO's say 'red' for protests' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Activist Kapito says demo does not make sense: Malawi CSO's say 'red' for protests' to a friend
Malawi national football team, the Flames’ coach Young Chimodzi and his deputy Jack Chamangwana have gone five months without pay....
Talk of disasters now not meaningless demos. Mungofunapo makobili basi mwauponda. Kasamaleni anzanu akubvutika ndi madzi.
A police thanks for increasing numbers of the demostrators ikanakhala one man show ndangodusapo
what do people expect from.this idiot Kapito who after being bribed by DPP as board chair of Southern Region Water Board. Kwathu kuno ndiye usadzabweretu. He is a greedy person uyu afunseni ma staff a ku MHRC akuudzani zambiri yamkulu ameneyo. Bungwe lakenso mdi one man band komanso nepotism ikumkhudza chifukwa anapatsidwa mpamdo chifukwa ndi mlomwe
Ndiye muyisovatu mvula yake imeneyi? Mmayetsa chani.mukufuna u president?dikirani 2024 panopa ba kandani choncho
a Kapito aphunzitseni a nyanchanja omwe akufuna kubweretsa chisokonezo mdziko lino.Gmd will not bless those demonstrators.
lero kuno ku bt kulibe olo munthu pa stadium. tiuzeni mulipati? ndikufuna ndidzaone osati ku marcha. cso mulibe anthu. mavenda akana
Expect little or no turnout out.I’ve seen a lot of people going for their daily routine activities and not bothered with this demo.It’s a low morale demo.CSOs please focus on real issues other than this.
kapito udindo wanu ndi wa long life?
Mulungu tifuna chitetezo chanu kwa ife ana anu kaya Mademo achitike kapena osachitika ife tidalila inu mbuye wathu titetezeni.
Bravo Kapito