Email a copy of 'Activists accuse MCP candidate Gwengwe of marrying a child bride' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

25 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Ineyo
Ineyo
6 years ago

If it’s true kuti anaterodi abwanawa then chilungamo chiyende ngati madzi basi so zandale apa

Fair Play
Fair Play
6 years ago

hehehe Gwengweyo anali ndi zaka zingati momwe amakwatira kamwanaka? ana okhaokha anakwatirana apa hiyaaaaaa!!!!!

Nganya
Nganya
6 years ago

Apa a Gwenge analakwisa. Ngakhale mwanayu anali wa masiye, sichifukwa chomukwatirila aliwang’ono, akanamupasa sukulu ya ulere chabwino ndikuzamukwatira akakula. Any way, madzi atayika titani.

nyenyezi
nyenyezi
6 years ago

Palibe chiona ine chanzeru apa osangonena kuti akudyetsani banzi a DPP bwanji? Nthawi yonseyi munali kuti mwaziwa lero? Cheap politics ngati mukufuna maudindo uku chimanga akupatseni munjira ina osati mwakamba apazi, nanu a Kamangira umphawi wakuvulazani eti kusowa zochita kumeneko, kafunsireni ntchito muzidyetsa banja lanu osati zimenezi

mjiba
mjiba
6 years ago

izi ndi zovuta kulowelela mulekeni Gwengweyo ayankhepo yenkha. Mulekeni abwele poyela kuti anene kuti mkazi wake, kaya kumene anapeleka mimba ali ndi zaka zingati? Kodi ndizoona kuti mtsikanayu anali pasukulu yake ya Gwengweyo ndipo anamupasa mimba ali ndi zaka zosayenela kukwatila malinga ndi malamulo a dziko lino? Nanga pokuti Gwengwe akufuna kuyimanso ngati MP kodi mchitidwewu azazuzula bwanji pamene iye ali patsogolo kugona ndi wana ndi kumawakwatila. Kodi chifukwa choti ndi olemela alibe mlandu pokuti akuuyimila Malawi Congress Party? Kodi chipani cha MCP ngati chikuvomereza mchitidwe umenewu ndiye kuti atsikana azatetezedwa mudziko muno chipanichi chikazalowa muboma???

Nadzimbiri
Nadzimbiri
6 years ago

akusiyana chani ndi Eric Aniva?

Kanthiti Mzandu
Kanthiti Mzandu
6 years ago

Booking for the room for press conference, paying journalist, paying inu o lankhulani buying fuel for vehicles used,and for the security aaaaaaasha iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii aaaaaaasha koma chiboma ichi kuononga ndalama zonsezo bwanji osagulila mankhwala mzi pat ala, bwanji osagulila magalimoto a Police kuti azipangila ma patrols, bwanji osakonzera madzi ku 18 komwe anthu alikumwa matuvi/manyi/nyasi koma chiboma ichi aaaaa

cashgate
cashgate
6 years ago

That’s not activism ; can Nyas times find another term for this stupidity? So at this present time are there still ppl who still think they can get away with this mediocrity? Indeed stupidity is a gift but DPP pliz don’t misuse your stupidity kkkkkk

Jamax
Jamax
6 years ago

Too late to bring such accusation,,,, 2015 is 2 years and I think she has a baby now,,, ok if this is true then let the child continue enjoying the family life as she is grown up now.

Toka
Toka
6 years ago

Akutumani eti? Mbuzi zachabechabe.

Read previous post:
Malawi Police arrest woman for husband’s murder in Ntcheu

A 31-year-old woman is in police custody in Ntcheu district on suspicion that she had a hand in her husband's...

Close