Alipila kwa munthu koma as rude as he is he can not even notice that the comandment says thou shalt kill. As such he will not confess to God. Hell is waiting. A rude person ,his desire is always to kill a person. He will continue doing this for life. No time to confess. shame of Kaka. He is a permanent person on earth? Kamuzu wamuyaya died. So who is kaka, will meet those he kills
oweluza alipo zikungodikilamnthawi bas inuyo zitinamizan
Aganya
8 years ago
Nthawi yonseyi amatani naye? Akuyenda mwa ufulu osaopanso wina aliyense nde pano mukufuna kunamiza ndani? Ali pa new lands pompa koma free man and yet it was murder pamene wolanda ma fon mmisewumu analowa kalekale. Mukungofuna kunamiza a Malawi, uyu sakalowa ku ndende. Atamupha mzakeyo ananena openly kuti samangidwa ndipo ndi zoonadi ndi mfulu mpakana pano. Ayi tiona.
wamubithazi
8 years ago
Why do Malawians like glorifying thugs just because he happen to have some spare parts shop in Bt?Its time he was rotting at Chichiri prison and the keys thrown in Mudi river.
o-deal-o and loot-epo
8 years ago
kundende ndi kwa amphawi. sangalowe ameneyo, analipila kale

Zwelithini southerner kikikiki sounds strange
GOING TO JAIL
Apa amalawi tafikapo tsopano bwanji boma likhazikitse lamulo loti opha mzake nayenso aphedwe kuti anthu tiziopa kuphana
Uyu munthu aoneka kuti amavala cithumwa mumusana kuti cizisokoneza ma judges muma court.That’s why amawina milandu yosiya-siyana.
Kama pamalawi pano zilipo eeeeish