Email a copy of 'Another person with albinism killed in Malawi: Thyolo businessman on the run' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Another person with albinism killed in Malawi: Thyolo businessman on the run' to a friend
Both academic and support staff at Mzuzu university have fingered the institution’s seven-member management for the financial woes ravaging the...
kulibwino titengete lamulo Manja mwathu,ameneyo timunyonge tokha akapezeka,akapita ku polisi awononganso ndalama za boma.
Pipo of this Village akumva munthu akulira why rushing kwa Mfumu. RIP Sunganani as these pipo also take the blame. Sanaganize bwino anthu amenewa, sob sob
it looks as if this is the epicentre of Albino killings. Apparently this minister involved in “maize gate” is looking for charms to soften the heart of HE so he is not fired. Thyolo people, why you, when the country’s leadership has condemned these acts. Is this how you are preparing for 2019?
Taikani chithuzi cha buzinesi maniyo. Ife naye ameneyo. Ku court chani apa. Anthu amenewa alibenso mantha pano kaya ku Joni tili naye naye.
Anthu a mmudzi anaganiza bwanji?akumva munthu akulira mnyumba iwo akuthamanga kaye kwa Mfumu,osangothyola nyumbayo bwanji?Life serving has no cost,reporting to the chief could have come second.RIP Sunganani Pensulo.
Anthu aku Thyolo thinking capacity ili low. Sangaganize mmene mukuneneramo. Ambiri ngosaphunzira. We need ka trong intervention ka education kumeneko!