Email a copy of 'APM christens March 18 as Malawi Day' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

10 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Mphondo
Mphondo
8 years ago

Malawi needs a Malawi day twice a week if things are going to change.

Akungolonje
Akungolonje
8 years ago

Ndiye zachiMalawi zimenezo pakuti ndi zodula kwambiri a Malawiwo maka ma civil servants azizipeza bwanji poti ndalama ndiye mwaikhwefula a Pitala, ma salary kuonjezera ngati momwe mzanu Joyce amachitira njeee!. Za mkutu basi, mwasowa zonena a President.
Alangizi nanunso ndiye mbatata zenizeni za anthu,….. Kuteroko mmati mwamulangiza zaphindu mzanuyo?

Chengolopiyo
Chengolopiyo
8 years ago

Kodi kachasu ndi illegal brew mpaka lero? Komatu zibwana zimenezo. M’mene amakomeramo!

Chengolopiyo
Chengolopiyo
8 years ago

Finally!! Malawi is waking up to the importance of promoting local products. For centuries we have fallen for junk from abroad simply because it carries labels that are said to attract social recognition and prestige. Komatu tsopano mutiuze kusiyana kwa foreign products produced in Malawi and real indigenous ones. Chifukwa ine chaka cha mawa pa 18 March sindidzamwa Carlsberg koma kachasu wofululidwa ndi anganga anga kunyumba. Kodi kachasu is still illegal brew? Komatu zibwana zimenezo, m’mene amakomera kachasumo!

wo
wo
8 years ago

Malawi imene achina chaponda amati anachoka kunja ku United nations ndikubwera kudzathandiza dziko lawo mmalo moyamba full time businesses. They came with nothing just like pitala and they want to suck Malawians.

Bwampini
Bwampini
8 years ago

Fodya eti misala

bruce munthali
bruce munthali
8 years ago

Mutharika Day!

GVH KHOMBE
GVH KHOMBE
8 years ago

Why can the be be celebrated on world heritage day? Other countries like south Africa do the same

Myao
Myao
8 years ago

And yet he donned a Eueopean suit, at least dzitenje or dzikoka za chingoni wouldve made sense.
Look at his govt, always happy to contract foreign firms at the expense of local one and there he is telling us to act to the contrary, koma abale.

trevor manyi
trevor manyi
8 years ago

Fodya eti

Read previous post:
Gwamba, Onesimus deny Chinga’s song: Salanje says ‘stop the hate’

Malawi’s top gospel artists have denied reports circulation in some Whatsapp group that they had released a song for departed...

Close