Email a copy of 'APM delivers! Bullets, Wanderers get land for their stadium' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'APM delivers! Bullets, Wanderers get land for their stadium' to a friend
The decision by the governing Democratic Progressive Party (DPP) to boycott the presidential and running mates televised debates last month...
No, i heard the president at the rally, he said ‘i will build you each a stadium (sic)’ and not i will give you plots for your stadia. There’s a huge difference baba, so say again that he has delivered, not to me.
Olo APM atawina sangamange ma stadium amenewa. Akamanga mundzandidule mutu!!!! Ndalama za boma kapena zake? Zaboma sidzingatheke coz parliament has to approve. Zake mwina ngati walemera kwambiri kuchoka pa 150,000 dollars anali nayo in 2014
DPP boma a china ndi china adadi mukukwana simukutekeseka with what pple think of u true leader Malawi needs
Adad zikomo, koma simuwina
Hand over the tittle deeds to clubs…if not then it’s just politics….
How can title deeds remain under the Ministry????
Ma stadium onsewo okomera anthu a mtauni . Bola mukanasisa fertilizer kufika pa K15,000.00 , olo kufka pa K10,000.00 ndiyekuti munthu wosauka , khaya wolemera azigula popanda chovuta . Koma fertilizer wanu wamakuponi amene akulemera ndi anthu omwewo a chipani cholamula. Nthawi ya Kamuzu panalibe kudandaula za fertilizer ayi chifukwa zimayenda mchilungamo . Fertilizer wa makuponiyu athe. Kuyambira malata , cement , fertilizer , zinthu zimenezi ndizomwe munthu wakumudzi angapindule nazo zitatsitsidwa ntengo , osati za mastadium zanuzo.
A waste of resources. APM wont even be President after May elections, he should have made such commitments after winning election.
This is personal commitment by APM, I am very sure he will fulfill it whether voted back or not.
Mabgani mangani koma ife tikukhuzula pa mpando ulipo mdala iwe. Ndipo ndalama zake za mthumba mwako kapena za ifeyo?
Kameza could have been ideal for one stadium being located on m1 road. moreover ter are already other plans to have other stadiums within or near to the proposed areas. Think twice
Utterly rubbish ! Political points ? Malawi needs more than mere stadia. Come on people open your eyes !
Open yours first. Call me after that
Ambuyakowo amange koma voting ya ine sazayipata