Email a copy of 'Arrest Wandale, demands chiefs over ‘sovereign State’ calls: United States of Thyolo and Mulanje' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

17 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Think Twice
7 years ago

Do you know that tea is now the second on bringing forex in this country? The industry pays much tax to the government. An everage worker gets about 18000 in two weeks. The industry employs so many people and huge sum of money inform of tax is paid to the government. Think critically before coming up with issues like these. It is just my concern because other people can think like goats like this. Education is indeed important.

Chibojola
Chibojola
7 years ago

A Ngolongoliwa sindinu muLomwe chifukwa Petro akulephera kutchula dzina lanu, koma Wandale akumutchula bwino. Alhomwe, alhomwe!!!!!!!!!!!!!!

Zimandiwawa
Zimandiwawa
7 years ago

Mafumu umbuli. “Idle land [malo omwe sakugwiritsidwa ntchito]” Kaya bwinobwino pamenepa?? Malowa apatsidwe kwa ana anu, adzukulu anu. Mwachidule athu anu. Basi amangidwe Wandale! Mwasuta fodya wa boma???
Osangotitu zilizonse tikhale mbali ya boma. Mudzalolanazo kuzulidwa mwanotu zimenezi.

Tamuthandizani Wandale-yo akumenyera ufulu wabwino kt mbumba zikhale nipolima komaxo pokhala.

Muli dyooo mafumu aku Mulanje Ni Thyolo.

Nathan k
Nathan k
7 years ago

Ngolongoliwa atikwana heavy kodi ndi mfumu or wandale walowa lit ufumu ameneyu

Kanchenga
Kanchenga
7 years ago

Kupusa a lomwe ife Kasungu Kamuzu atangotenga boma analanda achina Barrow malo onse amene amangokhala ku katunda chizinga kandawula. Mtunda kuchokera kwa kawamba kukafika Kwa Nyaza. Thyoloyo kuchepa. Lero aKasungu akulimamo. koma inu President wa ku thyolo wanu wanu kulephera kukambirana ndi Ma estate kuti inu mupeze polima. Mantha ndi azungu. Mfumu ndiye nkumati m’mangeni Ameneyo. Negative uzilu werewo bolanso midyomba page mangochi.
.

Zoona
Zoona
7 years ago

The proposed name itself tells alot. Komanso mumutengenso Peter wanu ife watikwana.

Dalitso Mpuzeni
Dalitso Mpuzeni
7 years ago

Why should he be arrested you idiots? Ngolingoliwa is beginning to bahave bigger than Malawi and thinks he has the power to command the police to arrest people, ufiti chiyani? Leave the man alone you idiots.

Phwisa
Phwisa
7 years ago

Really arrest Wandale for causing bleach of peace amongst not only residennts of these districts but all Malawian. That again tantamount to treason

Absalomchiwanda
7 years ago

Mafumu Opanda Nzeru mukufuna amumange Wandale chifukwa chani? Kanidi ndinu Mbuzi eti? Amumanga pa Mlandu woti Chani? Munthu kukhala activist ndiye Mpaka amangidwe? Inu osangomusiya azichita Yekha zakezo bwanji Mpaka atope????????/ Mafumu A Mulakho Kudontha kwambiri pamodzi ndi Mbwiyanu opanda Mano Mkamwayo kkkkkkk

Kanyimbi
Kanyimbi
7 years ago

Although I do not support Wandale, but these are the most foolish traditional leaders not only in Malawi but Africa. By the way do these chiefs have customary land to distribute to their subjects? They sold all the land. So instead of apologizing to this new generation that has found no land, they are disowning their own descendants. Foolishness at its best. ine sindimasekerera zopusa. Mapazi anu.

Read previous post:
Zodiak hints Facebook identity thieves

Private broadcasting house, Zodiak have been dealt a technological blow after some people stole its Facebook identity and are publishing...

Close