Email a copy of 'Asu scores debut winner for Nomads, KB hold Bullets: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Asu scores debut winner for Nomads, KB hold Bullets: Malawi TNM Super League' to a friend
Mzuzu University Football Club has got off the mark registering their first win in the TNM Super League after beating...
Iwe Asu za chimizi zakozo kwanu konko! Zovula jersey zilipobe? Uzavulenso game ya bullets, uzaone. Mwana wapa tchire iwe. Shupiti zako.
Mponda, your kids are good but they are not physically matching the super league crocodiles. You will end up being king maker, mark my words. You cant do anything. Wait for another disaster this week end. Vuto anawo akupasidwa ndalama zambiri zedi ndipo akudya wokha.Mponda osatengako anzako amatimu ena monga Anong’a. Azinyetsedwa choncho kuti ziwawawe zedi.this is not Nsenjere legue at all.You are not in biblical land where you can take only Davids to fight Goliaths and expect to win. No, no, impossible.Even David himself did not win out of blue, he used a tactical move by catapult with big… Read more »
KODI A MALAWI FE TINAKHALA BWANJI , NSANJE / KADUKA WALAKWA CHANI ASU?
Bullets held KB not KB Held Bullets, Plz you should always tell pipo the truth also in a right way.
inu a nyasa, pakati pa kb ndi bullets who held the other? i thought BB, IS THE THE WHICH HELD KB, GO FOR A REFRESHER COURSE SHUPITI
CHONDE EXECUTIVE KOMANSO TECHNICAL PANNEL YA B 4 WARD AUZENI MA PLAYERS KUTI AZIKONDANA ,MPIRA WOMWE TINAMENYA NDI SURE STREAM SAMAMUPATSA MPIRA STRIKER ATSU .AZIWE ICHI KAYA WACHINYA NDI NDANI KAYA NDANI POMALIZA IMAKHALA B 4 WRD IMENE YATENGA MA POINTS ONSE CHONDE .NDINE SAPOTA WOKHUDZIDWA
How good is this Ausu? why running half the pitch? why bowing to the coach? why giving the coach your arm band? why celebrating wildly as if its a cup final match winning goal?. Why taking off the shirt?. phweeeee. Ma why wa, ngochuluka zedi.
Bwanji sanaimbire Mpondayo game
shupit agalu inu chigoli cha offsyd muti bowe!mukondwelera poti wachinya ndi foreigner ymwe kwao amasewela chkulunga?akadzachnyaso foreigner wanuyu mudzandifuse
Mponda was bata uyu