Email a copy of 'Atupele ‘resetting the button’, to hold UDF rally Sunday in Bangwe' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Atupele ‘resetting the button’, to hold UDF rally Sunday in Bangwe' to a friend
As one way of informing, educating and entertaining people in the country, Lilongwe based renowned art theatre known as Dzuwa...
Santana Mbuli yeni yeni.
Atupele need to stand as UDF candidate so to put a bar from MCP in the region.
MCP should acknowledge that it is the same UDF which has thrashed you in Mangochi Malindi.
Atupele Sali serious payenkha wadyela plus corrupted, basi kumagwila ntchito ndi chipani cha anthu akuba(DPP)Just becouse iwe walandila undindo wa u minster plus kutchigiliza Kuti nkhani Ya Bambo ako yakuba isapite patali?
ATUPELE LET ME TELL YOU
EVEN IF YOU CAN GO AND STAND
AS A COUNSELLOR IN YOUR HOME VILLAGE YOU WON’T MAKE IT;
WHY ??
YOU ARE NOT SERIOUS WITH LIFE
YOU TAKE PEOPLE FOR GRANTED EVEN YOUR FATHER WON THE RACE COZ PEOPLE WERE DESPERATE FOR CHANGE
NOW AM SORRY YOUR CAN’T
MAKE IT EVEN IF YOU USE ALL THE
JUJUS FROM KAPOLOMA OR ALL
VITA BOOS ; FORGET !!
Kkkkkkkkkkkkkiest mpaka juju wakwa Akapoloma! Muchezeni bwino baby kkkkkkkk
Mwana uyu mmutu mwake mulibe nzeru, unagulitsa UDF ku DPP pano uzinamiza anthu ku ma location kuti UDF idzawina chisankho, ukawafunse a bambo ako kuti UDF unatha bwanji akakuyankhe wamva!
Obaba JZU Tembo papologilamu ya tiuzeni zoona pa zbs poyankha za mpungwepungwe mu mcp adati ndale zimafuna experience. Munthu singoti balamanthu wati ufuna upulezidenti. Anzungu sadalore kuti kamuzu afikile pampano wa upulezidenti. Adayambira kaye unduna mukabineti yawelesike kenako anampasa upulezidenti. Big Muluzi adayambila unduna kenako upulezidenti. Bingu adali nduna mukabineti ya udf kenaka pulezidenti. Joyice nduna mudpp then vp then pulezidenti. Pitala unduna then pulezidenti. Leader of opposition sadakhalepo pulezidenti chiyambire ulamuliro wa demokilanse. Mphwanga Atupele limbikira zabwino sathamangira zimabwela zokha.
Samuel ukunama tu iwe. Trump anakhalapo nduna kuti akhale president? How about Edgar Lungu of Zambia? Ndale za ku Malawi zotsalira kobasi. Mukodzedwa ndi kunyera komwe mpedzepedze May 2019. Chakwera ndi MCP akulizani chaka chamawa sizinaonekenso. Ulibe nzeru!
Atupele, are you serious with your becoming President one day? If yes, then why did chose to associate yourself with the beasts? Look now you have a hill to climb. Will you climb it successfully?
YOUTHS WAKE-UP !!
THESE FAMILY PARTIES WILL
TAKE US NOWHERE !!
THIS IS 21ST CENTURY
WE HAVE TO BE VISIONARY
LIKE BUSHIRI MAJOR 1 PHD
In as long as UDF is some “prostitute” relationship disguised as a marriage of convenience, it will never be seen as an independent party. In fact it’s association with DPP is it’s archilles heel. It will die with its partner party come May 2019. Whilst the marriage of c0nvinience works for you, honourable Atupele Muluzi, it certainly isn’t working for the party and the people of Malawi.