Email a copy of 'Atupele sets the tempo for Malawi 2019 elections: Addresses supporters at UDF headquarters' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Watipa
Watipa
6 years ago

Too late, MCP for change

I dont know
I dont know
6 years ago

This is the guying who is completely confused. He doesnot know what he wants in DPP let alone in UDF. If you want the party to be strong why sell it to crocodiles (Dpp). Atupele you are so opportunistic, you take malawians like cartoons

Mchape
6 years ago

Resign first in the cabinet mwana wa mbava u want to increase ur bargaining power mugwela limodzi ndi goodal gondwe and nankhumwa mbava inu ana a mfiti Mia sakusiyani muvina agalu

Neno
Neno
6 years ago

KKKKKK….Like father like son zowonadi…Yathano five years mwayambapo…Munalitu chete inu ngati simumawona

CHIPYERELO
CHIPYERELO
6 years ago

My good friend Atupele consider your chances in the presidential elections very slim

pathfinder
pathfinder
6 years ago

Kodi inu a MCP mmangolubwalubwa, mudzachititsa liti kapena atsogoleri anu adzachititsa liti msonkhano, kuti tadzaone anthu ochuluka chonchi? Kapena tinene kutinso atola nkhani a nyasatimes ndi onga a MBC kuti akukukhomelerani, safuna kuti tione masapota ochuluka pa misonkhano yanu?

Mwinithengo Azidya Papakulu
Mwinithengo Azidya Papakulu
6 years ago

Bambo Atupele mwapusisa anthu kokwana.Chipani chisamakhale ngati choopsyezera mundale kuti muzipeza timanakinaki.Pano cabinet reshuffle ili pafupi mukufuna anthu kuti muzitolere.Mwadusitsa ma bill achabe ndikuzapondereza electoral reform bill kuti muzidya nawo ma cashgate wo.Pangani zomwezo kuti mudyenso ka 4billion kaja ka Goodall Gondwe ndi Nankhumwa.And mwakanikatu kuuza anthu zomwe UDF pachisankho iyima yokha or Ndi banja lanu ndi dpp?.Facebook ndi Whatsapp tiuzeni zomwe muli?Tisamangotengerana muthumba ngati malonda amphaka.

Nabetha
Nabetha
6 years ago

Mwana osapola liwombo komanso pa mchombo uyu. Moti iyeyu sakuwona kuti dzanja lalemba khoma. Moti baby ameneyu sakuwona kuti Lucius Banda naye akayambapo zake ndiye kuti mphepo ya mwera yalowa muchipani. Plibe munthu amene malimba ndi mphepo ya mwera.

Read previous post:
MCP says not party to ‘experimenting with people’s taxes’ in K4bn MPs dubious funds

The  main opposition Malawi Congress Party (MCP) has changed tune in the  K4 billion “funding by-pass” which was allocated to...

Close