Email a copy of 'Atupele to set the ‘new beginning’ tone for Malawi 2019 elections: Rallies in Balaka North, Machinga South East' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Atupele to set the ‘new beginning’ tone for Malawi 2019 elections: Rallies in Balaka North, Machinga South East' to a friend
An award winning Malawian Afro-pop musician, Shukuran Mwachumu, well known as Janta, is set to release a new song on...
Was a die hard wa UDF
Pano or mbuzi itavala salu
Sindiku votera manyaka achipani
Panooo ndine wa UTM…………
It bowazi me so much ndikamava za atupele & used UDF…
Atupele DDP ikusangalala chifukwa ya zimisa UDF
Unalakwisa kulowa DPP iwe
Unapha chipani…
Lero UDF ilibe voice…
Usati bowe ife atupere
Tinaku topera
MA games ako ndi chindere
Upeze oti uzanamizi
Or mbuzi itamwa tea iwe sunga wine
Atupele wasuta kanundu chani? Koma mwana uyuuuuuuuuuuuuuuu uyu mwana uyuuuuuuuuuu………………………………….. pano ulidziwa dziko ngati umaganiza kuti zimene anthu ankanena kunali kudana nawe mphwamgaaaaaaaaaaaaaaa!!
Waona njoka yasato mmene imamezela wamoyoooooooooooooo munthuuuuuuuuuuuuu!! Lero dpp yakutsitsila pa njira, utsi tolo galimoto ya dpp kumapita iwe ukuonaaaaaaaaaaaaaaa……………………… mwanayoooooooooooooooooo
This guy is never short of phrases. Its “rebranding today” ,”revamped tomorrow ” and ” new tone” next day. You can fool. some people some of the time but not all the people all the time. UDF time is up
Going by the comments, I think this man has lost it all. Someone who would want to be elected president of a country in 5 months time and he is still peddling policies of another party, can he really be taken seriously. Also with reference from the results of the last election Atupele should not have even joined DPP. Tulo achawa. Ndiamene akutiwonongera dzikoli. A DPP akunenetsa modzikonda kuti tagwetsa UDP ku Eastern Region iyecAtupele alipompo duu, ndiye kuti mutu umagwira?
Atupele is fake. He is always under the armpit of DPP. We can’t trust him. Ukhuluku basi.
Atupele ndale munalowera kuteteza bambo ako kuti asamangidwe. Akuvotera bambo ako omwewo
The other time he said he had a winning joker card for 2019 elections. Kuwatukwana kapena kuderera a yao kumeneku. Zoti ndikhoza kupanga zimene ndikufuna ovota alipo kale ndidzakhalanso prezidenti wa UDF mpaka kalekale. Ndiye anthu amawawuza chiyani?