Email a copy of 'Audio of Wa Jeffrey phone call with Nankhumwa on DPP cracks goes viral: Full transcript' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Audio of Wa Jeffrey phone call with Nankhumwa on DPP cracks goes viral: Full transcript' to a friend
An editorial comment in flagship weekly, Malawi News says the assault on Times Group journalist by Democratic Progressive Party (DPP)...
I have picked one statement from the transcript : NK: “But the President doesn’t listen to anyone.” Like brother ..like brother. Azipita. We should not be blaming anyone– but the president. Nankhumwa has said it. Professor professor wachani. From mkalasi to library then home. Osacheza ndi anthu. He has to go. So, please don’t blame any of his cabinet members. This guy never expected to have such power after being a professor in the USA. Those of you who have studied in the USA, you will understand what African professors go through. This guy thinks he is the only intelligent… Read more »
Apa ndiye ndale zabeba. Ku DPP kwanunkha mtope man. Agwape anabisala pa tsamba LA mtedza. Mungaswere ndi Saulosi mnyamata wa IT? Mudziwanso. Even APM wanuyo Amadziwa bwino za SCK. Apa Ndiye ndale zikukoma. Pofika 2019 Kaya kukhala zotani. Ine anga ndi maso. Mumayenda mphepete mudziwanso
It is a shame when leaders surround themselves with this calibre of people. How can we develop as a nation?
Crocodiles that control Malawi. Evil men
Ntchito za anthu ena nzosagwirizana ndi ndale. Mulungu amapeleka maluso osiyanasiyana kwa aliyense. Ena asangalatsi, ena atsogoleri, ena andale. Asangalatsi aliponso mmagulu osiyanasiyana ena ampila, ena oyimba, ena zisutso, ena alakatuli, ena makatuni. Makatuninso alipo osiyana ena anyuzipepa ndi ena apakanema. Kubweretsa anthu amenewa mundale ndikupha dziko komanso kusalifunira dziko. Why? Amalubwalubwa zambiri kenako anthu abwinobwino mumayambanso kulubwalubwa. Ndivomelezane ndi Patricia Kaliyati APM adalakwila mtundu wa amalawi pobweletsa Saulosi Kilaulosi Chilima kundale za dziko. Saulosi ndi katsiri wa makatuni. Amatha kujambula Mtengo, Kalulu. mkango. zonse zopandamoyo koma muluso lake lapakanema zimaoneka kuti mkango ukuthamangisa kalulu, kalulu akukwela mumtengo. Mkango ukufunsa… Read more »
Achimwene ziko liri pa mavuto chifukwa APM alibemphatso ya utsogoleri anta.Ndi Unduna uti anapasidwa ndi Bingu anatoukwanitsa?
Ndale zanuzo zikusokoneza mtendere pamalawi pano. Mukuchita ngati Malawi ndi DPP. MCP kapena AFORD bwanji? Mungokangana ndiye tikupaseninso boma zitha bwa? Anthu oipa ntchito zao ndikubweretsa ziwawa mdziko. Tisiyileni Malawi wathuyu we can do without you. Maso a anthu 17million sangaonenne chimodzi modzi. Ngati president akulakwitsa yambani chanu chipani. Pangani kampeni yanu. Amalawi akakhutitsidwa adzakuvoterani. Osamangolubwalubwa ngati anzeru ndinu nokha. Mukambirane muzipani mwanu. Mukapikisane kukonveshoni owinawo adzapikisane 2019. Oluzawo athandize anzao owinao. Ngati sakufuna konsititushoni ya Malawi imalora kujoina zipani zina, kapena kuyamba chanu chipani mukazithemba, kapenanso kuyima pawekha (indipendenti kapenanso kungokhala. Zonsezi malamulo amalora kuletsa zimene mukuchitazo. Tizingomva DPP,… Read more »
The same big mistake Mluzi did when he brought a big crook Bingu wa Munthalika to udf like they were no potential leaders in the party. Did he sort the problem after Bingu became greedy and abandon the party that gave him a lifeline? It was a big NO, he went on to sacrifice his son and that was the end of that cartoon movie. Oyenda ndi lupanga amafanso ndi lupanga- this is just the beginning.
YOU THINK YOU COULD JUST DUMP CHILIMA LIKE THAT? YOU MUST BE JOKING! TIMANGOKUONANI IFE. ZANU IZO!
DPP HAS GOT ITSELF TO BLAME. THEY SIDELINED CHILIMA AND THEY DID NOT GIVE HIM ANY POSITION IN THE PARTY. THAT IS WHY HE IS FREE TO PENETRATE THE DPP AND CAUSE HAVOC. HE CANT BE BLAMED. ZINTHU ZINAZI ZIMAFUNIKA KUZIONERA PATALI. NOW THE DPP RISKS SPLITTING THE PARTY. THERE ARE SO MANY DISGRUNTLED SUPPOTERS WHO ARE BACKING CHILIMA. MUSOVA!!!!!!!!!!!!!
MBAVA ZOOPSYA NDI ZOLUSA ZIKULAMULIRA DZIKO DZAONONGA MALAWI. MEC TIKUFUNA CHISANKHO CHAKA CHOMWE CHINO NOT NEXT YEAR. TIPULUMUTSE NDALAMA ZATSALAZO NDITHU. GOVERNMENT UNDER SIEGE BY DANGEROUS THIEVES LED BY THE PRINCE HIMSELF
They don’t even know how to protect themselves from eve’s droppers. Onyo mwapezeka. This is a high tech generation. Nkhalamba nonse mumva mbebe chaka chino!!
It looks like Jeffrey has no eyebrows ……….only a pencil line! Latest fashion perhaps?