Email a copy of 'Baba to Nomads move in twist and turns: Masters in contradictory claims' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Baba to Nomads move in twist and turns: Masters in contradictory claims' to a friend
Malawi Police Services in Lilongwe have arrested two Sri Lankas after they were found with precious minerals including copper without...
GS was supposed to consult his boss first. Munthu akuyesesa kutukula masewero ampila sibwino kumukhumudwitsa chifukwa chadyera. Nzanu wavutika kukamtenga player kunja, kumusula inu ndiye mudyelere iye osadziwa? Kulakwatu kumeneko. Musaphe Masters. Tatopa kungomva za Maule, Nyerere. Tizimvako matimu achimalawiwa mtokwa, masters, mponela, karonga united kuti suuper league yathu ithe kusula maplayer opambanisa Malawi the flames. Enawa akugulira dyera kuti kompitishoni ichepe adzikathera pabenchi. Where is Jafali and others?
Gangata watumidwa ndi Haiya!
Malawi football, Man U sold CR7 to Madrid when he was at the pick and RM sold him again to Juve you can’t hear disagreements in their deals, why hear in Malawi? You hear of Chande, Sambani etc
dont compare CR7 ndi zinthu zopusa