Email a copy of 'Baby dumper ordered to do community service' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Baby dumper ordered to do community service' to a friend
President Peter Mutharika has told global leaders meeting in New York, US that he was elected Malawi’s fifth Head of...
Mayiyo mmene amakwerana nd mwamuna wakeo samadziwa kt apanga mwana,amangomva kukoma bas! Zitsru zawanthu!!
Nkofunikanso kuti bamboyo alandile zikwapu 1111 komanso azile ndi kusuka mite go 111, pomaaliza amwe mazi ndowa ziwiri osapumila, apo ayi akakhale pa shamba Ku chichiri kwa zaka 4.
Koma chisoni ndithu…mwana 3.8kgs kumutaya,anzanu abereka WA 1.8kgs uyu akupumayu
Komanso Bambo wake asese 20 hours kuti asamapereke Ana kwa anthu osasamala. Inu zowona
mimba kumamangopereka kwa amisala. Mmene kumavutila kupanga mwana muja.
amayi inu …need DELIVERANCE ndithu
Concealing death is a misdemeanour carrying a sentence of 2 years not 5 years imprisonment.
Wanangwa and Viva Nyimba. The names tell it.
If she belongs 2yo family rit. I dnt agree wt u a judge v dis matter. U better jst pool ha cold water unlyk kunyengeza anthu kt mwapeleka chilango. 40hrs community service? Shame on u Mr Judge
Dzomvetsa chisoni kwambiri kodi akhothi mumanya manyi pogamula mulandu kamba chani? kodi simoyo umenewo amautayao, komwe kuli kupha, tsono kachilango kameneka inu eni mukuti mwalanga? gudge wopusa iwe kwambiri ndipo sukudziwa kuti uli pamenepo kamba chani. Ndakhumudwa kwambiri iwe usiye mtchito.
Kod ma judge enawa ndi dzina lokha eti?kachigamuloka kachepa mayiwa amafuna kupha amayenela kulandila chilango chowamvexa kuwawa.