Email a copy of 'Bagus quits MCP, repositioning with DPP: Mia wishes him well' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bagus quits MCP, repositioning with DPP: Mia wishes him well' to a friend
Aniya Phone, winner of the 10th draw of the MK1 million Airtel Bandulo Bandulo competition intends to make very good use of the...
Inside information says he will NEVER re-join DPP. FAKE NEWS!!
A Humphrey, Mia wake uti? Miayo analowa kongilesi ndi cholinga choti aphukire ponamizira kuti akutolera ndalama za chipani. Lero khoswe was m’chalitchi Ali ndi khusa kuposa Mia.
Joining dpp thieves? Mutu ukugwira ntchito? Kungoti ma K145 million a Zameer and magalimoto aphweka basi you decide to go back. Pitani kadyeni misonkho akutibera Alamu Pumani Mwakula.
Irrelevant politician.
He was just relevant few months ago when he joined MCP. All of a sudden now he becomes irrelevant becomes he is resigning from MCP. Hahahaha
Mercenaries in MCP thanks to Chakwera and his band of nomads.. Open your eyes Reverend,only close them when you are praying,mubetsa MCP
Any person with democratic credentials cannot work comfortably ndi kongilesi. Amene sanaphepo munthu sangakhale Ku kongilesi. Bagus congratulations for disassociating with murderers.
chasowa Robert and all others si anthu eti?
Kumeneko nde timati kupanda nzeru, kuganiza mopelewera. A pumbwa mulipo ambiri. Mmesa dzigawenga dzimene dzinkapha anthu dzinabwera ku DPP kwanuko. Pano dzinakaphabe anthu osalakwa, the likes of Njauju, Chasowa and the list goes on
Who is bagus?Ichi lakula ndi dyela komanso umphawi nangasi adamuchotsa pa udindo Ku bungwe kuja,,,,,Ku DPP akufunako ndalama koma walemba mmadzi
Kkkkkkk amaona ngati adyera Mia
JUST QUIT POLITICS OLD MAN –THE GAME IS IN THE HANDS OF YOUNG VIBRANT INTELLIGENT LEADERS WHO CAN TAKE MOTHER MALAWI TO GREATER LEVELS NOW
He is only actually 56 Years old. Probably still one of malawi’s youngest politicians. Check your information before commenting!
Lower Shire is voting for the DPP enmasse…..Bagus waionela patali game