Email a copy of 'Bernadetta Mlaka Maliro launches ‘Yahweh’ album in style: Lucius Banda spices show' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bernadetta Mlaka Maliro launches ‘Yahweh’ album in style: Lucius Banda spices show' to a friend
The people of Mangochi had a double celebration on Thursday when Airtel Malawi opened its new state of the art...
Mr. Chilangwe, it appears that you don’t know. Mlakamaliro is one name and Bernadetta’s husband is called Macdonald. Musaiwale kuti kumalawi tili ndi ma surname oterewa ngati; Kachindamoto, Chiyendausiku, Zungulirakhonde, Nsaluyavuka, Mwalamoyo etc. Of course anthu ena amatha kudula mainawa chifukwa amatalika tikamalemba pa ma form osiyana-siyana, but it depends on one’s choice.
Amalawi nanunso,Mpaka maina onse amwamuna pa msokho,mukadaika dzina lanu la bambo anu kenako la maliro,kuyifela!!!!!!!!!!!!!
number 7 walankhula zooona supporting artist kumpasa mita ngati show ndiyake. Komabe aaa bigup soja unaivesa kukoma.
Mwamuchesula allan ngumuya mzanu waotchatu kunali anthu ochepa kaya azawinanso kaya ndskaika
sadzawina ndi2
Man Soldier mumaitha mumathandiza ku zandale MCP anthu kutokota, here you are Gospel thats the real life to go by Gospel is good, keep it up & next I will ask you ku zaimba ku Masanjala Parish CZ,will you
As your show, be the last to play not in between.. otherwise people rememeber the last artist forgetting that it is your show. So in LL and Mzuzu, be the last to play, even after a short break …just thinking on your behalf..make an impact ,,the others are just supporting artists!
madam mulakawa tisanamepo apa ndiokongola,,,mlaka unasankha axse
zabwino zonse anthu anakumbukra kale lanu soja akuimba pamodzi ndi mlaka
what I fail to understand is that launching an album happens only once there after are performances! what is wrong in Malawi? Is it fund raising?
Anasiya zijazi Bernadetta?