Email a copy of 'BJ wants Constitution amendment for President to have powers to fire veep' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'BJ wants Constitution amendment for President to have powers to fire veep' to a friend
Quasi- religious body, Public Affairs Committee (PAC) meets next week to discuss how the graft busting body, the Anti-Corruption Bureau...
I have been thinking about the same, we don’t need vice president here, Once I become an MP next year, ena mwa malamulo oyenela kusinthidwa ndi amenewa. Number of ministers to be fixed etc.
Mpinganjira anagwesedwa ndi nakhumwa. He will never be an MP again in Malawi. May be if goes to Mozambique.Bakili sanaminamizilre kuti wolanda akazi aeni ake. Mpinganjira kusauka mpakana kosowa pogwira ali ndimunyengerere nakhumwa amuuze APM kuti iye ndi wa DPP cholinga amunikhe kampando, ndi awa ali National Roads Authority. Munthu wopannda nzeru Mpinganjira. Ntchito kupempha zovala kwa achibale ali kunja.
Mpinganjira nanga akalakwa President anthu azitani?Monga pano bwana akowa aba ndalama tizitani?….
.Ndipo akuyankhula ngati ndani kuchipani?Chimene unapangapo wanzeru pamoyo wako kuposa kulephera chisankho nchiani?Munthuyu ndiomvesa chisoni kwabasi. Taonani zomwe akuyankhula zopanda nzeru ngati izo
…pano ukupusisa DPP kuti atenge chimunthu Banda chifukwa choti umadana ndi bakili miluzi.
Munthu woipa iwe. Siya ena alamule
Useless thinking Mpinganjira & who is Mpinganjira to think such a way that President is always right?
JB is right. That’s the only way we can keep a good relationship between the president and his vice.
Iwe leave JB alone. Uziti BJ.
We r crying of reducing the appointment powers of the sitting President ndiye wina is thinking of increasing those powers just bcoz anamupatsa u Chairman wa Roads Authority zoona a Malawi zimenezi? Shameful indeed
Mad person trying to give a wrong advice……. BJ palibe atakumvere iwe unatha longtime ago…moti wekha sumadziwa kodi
He can’t even win in his own home village
Well said! The change should also allow voters to fire the president any time during the five years if he/she iz on the wrong lane.
Thats a good one
Ndiwo umpinganjira umenewo. Zoganiza zake zankhanza basi. Ndiye mmene anawawongera amayi komanso bakili.
Why change a constitutional clause which ensures that there is respect between the two.
As a matter of fact, that is the only clause in our constitution that at least brings a bit of pride to us Malawians and guarantees that no matter how tribalistic (like Mpinganyere) a president can be, they can not toy around with an innocent sitting vice-president.
Akulu awa ofunika ku maula May 2019.
It takes wisdom to realise that your productive age is past gone. These people of BJ’s calibre are spent forces and should disappear from active political stage to pave way for vibrant young minds with fresh ideas to turn around things.
Malawi is the same old story which is embarrassing, abject poverty, abject poverty and abject poverty.