Email a copy of 'Blantyre derby in Capital ugly scenes, barren draw: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Blantyre derby in Capital ugly scenes, barren draw: Malawi TNM Super League' to a friend
Some businesspeople in Malawi have expressed dismay with the April 27 nationwide demonstrations, saying the closure of shops during the...
The officiating team was too biased. To me the last goal was an honest goal.
Mpira ku Malawi sudzatukuka ngati ma Ref adzipanga khalidwe lake limeneli,in true sense those were clear goals to me Ref anakwera ndithu all in all congrants to my boys,munaikirapo mtima koma Ref watikhomelera komabe ife Maule this year Super League titenga basi.MAULE MOTO KUTI BUUUUUUUUUUUUUUU!!!!!!!!!!!!
Uzayambe kuimbira iweyo
mmmmmmmm titelo kuti inu amene mukudandaulanu mukanasangalala akanalola chigoli cha off sidecho?? khalani sereous guys,,titukule mpila osati zachinyengo,kunjako tikamakayenda samalola za offside,,big up Ngoleka
Bullets 2 goals were disallowed why? ? Poor refree in true sense Bullets worn the game 2 to nothing. Refree mapazi ake
Ma ref aku Malawi ndi choncho kuononga game basi! !!!!!!! I think chinyengo chinalowapo ndipo zifufuzidwe bwino izi.