Email a copy of 'BLM promotes safe sex in new Manyuchi condoms: ‘Tseketseke for Life’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

56 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mphasayaweni lobi
mphasayaweni lobi
8 years ago

hahahahaha nanunso a Sarah zoona kupanga komenti zimenezi? tangofunsani ngati akazinso alipo makondomu, kuti uzigwiritsa ntchito.

nazimbiri
nazimbiri
8 years ago

koma ka mzungu angakayike mukondomu,wausilu mzungu ameneyu eti.anthu atopwetekana kondomu ili m’manja.kodi mwatosowa zonena eti?

Hamu
Hamu
8 years ago

Uchimo kuwuika pabwalo sopano!!!!!! Ankhu amenewa ayenera kuti akayesa kugwiritsa ntchito ndi azimuna awo makondomuwa, chifukwa ndi zodabwisa kunena kuti ndichokomesa chisembwere anakachiyese.

Sarah Kaligwenje
Sarah Kaligwenje
8 years ago

Comment Is This True?

ELECTORATE MZIKA
8 years ago

These are the agents of death cunningly promoting adultery,promiscuity and the HIV in the guise of safe sex, reproductive health and safe motherhood.

Arthur
Arthur
8 years ago

Eeeeeeeee guyz chakachino kuli kunyenga akazi ambiri…. Wina alira.

kd
kd
8 years ago

ife sitivala condom ndife achimidzi

NGWAZI ACHALUME
8 years ago

KOMA MANYUCHI MAKONDOMU ABWINO NGATI AWA SINDINAWAONEPO INE…. NDINAYAMBA KUGWIRISA NTCHITO KWA CHIBWENZI CHANGA CHOYAMBA NDILI PA BANJA KALE MPAKA PANO SINDINASIYEBE MANYUCHI….BIG UP BLM

Nkalapwaga
Nkalapwaga
8 years ago

Haraam

Juju
Juju
8 years ago

Amai Mitochi mubwere ku Big Brother tidzacheze, tiyese zimenezi basi tione m’mene zimako mera, nanga nkutani

Read previous post:
Malawi lose to Madagascar in beach soccer finals

The Malawi beach soccer team on Saturday endured a bad day in Seychelles in the first quarter of the  inaugural...

Close