Email a copy of 'BT united recalls Sparrow from Nomads ' to a friend * Required Field Your Name: * Your E-Mail: * Your Remark: Friend's Name: * Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries. Friend's E-Mail: * Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries. Image Verification: * Loading ... Sharing is caring! 0 shares Share Tweet Pin LinkedIn Email Print
Chamangwana kuumira nthumba,mpaka tiluze player wa bwinoyu
Iwe ngati uli ndindalama thandiza team osamangoyankhula mbwelera apa. Ngakhale muli pacampain yowononga team simukwanitsa teamyi ilipo mpakana kale. Ineyo sindidzasiya kusapota Noma.
Zoona Phiri zimene ukunenazo komanso 3pts yatoledwa.
Apa ndiye kukama yoonda mwachotsas sparrow aaaaaa nyerere kaya mwaaaa
Please try to square atransifer fee at agood time bcoz when the team is loosing don’t blame the coach blame the executive,i cry 4my nomads ooooh!!!.
Please try to square atransifer at agood time bcoz when the team is loosing don’t blame the coach blame the executive,i cry 4my nomads ooooh!!!.
izi ndi zintchito za kanyenda ndi yona malunga kusafunira team yao za bwino basi ikatha tiona chomwe muzichita ntchito kuba ku mpira basi
Atolankhan makutu akungokhala ku wanderers nkhan zkutuluka zonyasa zokhazokha kod ma trustee simukuziona zimenezi mwina masapota akamagenda mumakondwa eti ngat zavuta patsana captain amalize season excective ikapume tatopanazo
We want kanyenda back
koma manoma ntchito kuba ab-asi
Bolaso achina yona ndi mr kanyenda amayesetsa kugura ma player nt zachina chamangwanazi