Email a copy of 'BT United rejects Silver claims on signing Limbani' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'BT United rejects Silver claims on signing Limbani' to a friend
Composer of the National Anthem late Michael Fredrick Paul Sauka will be honoured by the organisers of this year’s annual Music...
That’s why ine will never suport bullets ana amasiye koma opanda ulemu. Kwawo ndi kuba kutukwana kupempha. Team mpaka season ikupempha? Enafe tikungosintha sponsorship ngati zitenje za mkazi wa mimba.
Typical of Malawians,Jelousy with other peoples success.Mupwisa utsi chaka chake ndi chino Bullets simungaithe ,ilibe anzao pa Malawi pano. Koma mukapitiliza inu a SECRETARY A SILVER TIKUCHITANI TINTINI MUMVANSO.
Utolankhani wa mike bango ngoseketsa heavy kuulutsa nkhani b4 investigation…..atolankhani ongowatola mmakwalala….MIKE BANGO WA SILVER UNYERA CHAKA CHINO IWEEEEE
Silver is jealous of Bullets’ recent exploits. You thought you are the best club on the land to the extent of refusing to sell your players to the people’s team.KhKKKKKKKKKKKKKKKKK! Whatever the case, you will never substitute Bullets mpaka Yesu adzabwera
Ndati ndiyankhepo pa nkhaniyi!!
Ine ndine wa Bullets,silver isakunamizeni kalikonse.ma fon Nde akumaimbadi Kuti akundifuna koma ndawauza Kuti anachedwa.andilonjeza zambili mpaka galimoto,koma mtima wanga ku silver sindingamenyeko mpila.the Only team in Malawi Where I can expose myself is Bullets!! So Silver GET OFF!!!!
Inu a silver lero muwafuna anzanu.suja pa dzana paja munkatumwa ndi chawanangwa wanu uja.Nanunso mwayandama mu thobwa
Noma ikumagula maplayer okalamba , chule Wadabwa ,James zakazaka, mwinanso Gilbert Chirwa
silver yapenga kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
live longer manoma let them talk bcoz they are poor due to their thievery activities when money is given to them
Anakoma mateamuwa amusiya Limbani, tione mwina mugulitsa kuti? Tangotchajani ena akupaseni makobili, Limbani is not a Nomber one player in Malawi, Eh kulimadolooo!
A Malawi sindife opusa kuti muzitinamiza. Ma club Mwaonjeza kunena mabodza and u r losing ur credibility