Email a copy of 'Bullets beat Rangers 2-1: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets beat Rangers 2-1: Malawi TNM Super League' to a friend
Shocked with the growing number of children dropping out of school,Traditional leaders in Mangochi have joined the Campaign for Female...
Chithunzi ichi ndichatsiku limene tinatenga chikho cha Carlsburg osati chaku Chitowe inu Mwamva?
Inu a NYASA musamatinamidze mwamva? Kumeneko ndi ku CHITOWE kapena pa KAMUZU STADIUM? Chonde mudziika zithunzi zatsopano. Zabodza ife ayi mwamva?
peoples team ndiyantwa
IZ IT JIMMY OR SANKHANI FIND OUT PLEASE
maule ndi chitimu man
MAULE NDIKUMVAKUKOMA
wawa mawule mumandinyadilisa or kuno ku sauth africa timaku nyadilani pitilizani zokomazo mmmmmmmmmmm koma palinso timu monga iyi?????????????????
Ine pheeee uziwe kuti bullets yandya wina koma bullets yimandivetsa ku koma
The pples team imadikira last whistle ndiye kuti game yatha osati wina kungotsogola ndi kachigoli kamodzi basi nkuyamba defending kapena ma delaying tactics, timabwenza ife nkutsogolanso ndipo aka sikoyamba muwafunse abambo ku azam
Congrats ma players athu a MAULE !!! That’s what ur supporters want. We want zigoli!!! Nothing else!!! Chaka chino tikutenga champions ndi zikho zina zotero!!! NB: Swazurimoh Ramadan yo asabwerere kusokoneza team yathu ikuchita bwino kaleyi. Kananji is already doing fine. No need to bring in a foreigner here. Ma samu a Kondi amenewo kuti adzidya kumbuyo kwa m’bwerayu!! Takanaaaaaaaa!!!!!!