Bullets is a big team, it was not supposed to lose against silver strikers? is silver a small team? Ndi mmene umakhalira mpila, ma supporters amene mumapangitsa ziwawa aja ndi inu, kusavomeleza kuti pena mpila timatha kuluza, inde zikutipweteka, koma I advise against that kind of thinking
chigolichina
6 years ago
Munya mukaluzanso or kupanga draw agwape inu zitsilu.
Anyamata musade nkhawa kukadali m’mawa kuluza magemu awiri ndimmene zimakhalira musataye mtima tiyamba kuwina tsopano
Bullets hooooooyyeeeee!!!!!!!!!
work hard on dis one ,adawise Bullets ndi big team yu were nat suppose to luz games ku mz and against. silvver strikers
Bullets is a big team, it was not supposed to lose against silver strikers? is silver a small team? Ndi mmene umakhalira mpila, ma supporters amene mumapangitsa ziwawa aja ndi inu, kusavomeleza kuti pena mpila timatha kuluza, inde zikutipweteka, koma I advise against that kind of thinking
Munya mukaluzanso or kupanga draw agwape inu zitsilu.
Ochenjera ndi inu timakunyadirani munthu wa mkulu. Mulungu akudaliseni pomwenso akuyang”anilira ife zitsiru monga mwa mawu anu bwana. Have a nice day.
ur representing the south, ur fighting a team from the central, so u lose u go to the central, `2 much.