Email a copy of 'Bullets can sniff title: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets can sniff title: Malawi TNM Super League' to a friend
Activists Billy Mayaya and Rev Macdonald Sembereka on Sunday accused Parliament for spending K300million in procurement of four State of...
BB mtima pansi cup ili m’manja mwathu aneba afune asafune
Tnm was made for bb bax
We Are the Champion (WAC) Bullets!!!
Tiwonana tilimmbuyomo. Linda madzi apite ndipo uziti ndadala.The Bankers kamuna bambooooo.
BB woooooyeeeeeeeeeeee, Neba muli mmadzi
Mwamaule zonse ndizotheka!!!.manyazi agwire aneba ngat satenga cup???.
By & by w’ll make it.aneba izooo!!!!!!!.
Well done our heros for the job mwatimvetsa kukoma, nkubweretsanso chisangalalo kubanja la BB, akanganya amalalata udyo, don’t think pano alinso ndi mawu, a word of advice to management pliz do not disappoint the players in any way or the other so as to give them morale to grab the championiship. Wamkaka maule tikumva pamene neba akumva wamandimu
Maule womwewo kukti wawa wawa wawa, neba ukumva bwanji mnthupimo, kodi ndiye watha mpaka number 9 achitenso kukuvotera ma kasitomala a Standard Bank, nkhondo sungazimenyere wekha? manyazi bwanji? Amene mumatokota pa fb last week kuti pali amene angaimenso pachulu kuti amasapota BB, tokotanitu? mayankho mukuwaziwa kale TNM championiship ikununkhiradi
Bullets timu ya wanthu wa chamba, kusasamba mkati.