Email a copy of 'Bullets crowned Malawi champions: TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

56 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Allan ngwesu
Allan ngwesu
9 years ago

Zikumuwawa akakolope nyanja Maule woyeeee!!!

Tate wa Tate
Tate wa Tate
9 years ago

Amene mukunena zamapoints omwe anakuchotserani chifukwa chauchifwaaaaaaaaaamba pa Balaka .TENGANI TIMAPOINTS TANUTO MUPHATIKIZIRE NDI TOMWE MUKULILIRATO mupeza nokha yankho. For the past 9 years no team has ammased 62 points mumangobwerera ma 40 mwina ma 50 ndiye mukufuna kunamizira chani? Tangoyamikani kuti It pays to be a Bullets fan,Tikusimbwa pa town!!!.N’kokoma kusapota Bullets!! Matimu ena amangoyerekezera Bullets ndiwo mizyanya,mphangala,mizozodo,Nzalamangwe za chikopa pa Malawi

n'jomba ulanda
9 years ago

anamwa tea azamwanso siizi… hehedeeeeeeee uuuuluuuuu

Khalamule
Khalamule
9 years ago

Bullets have always been champions only that some of you do not wish them well, Manyazi bwa? The team for the Nation!!!!,Peoples team!!!! ,ma Palestina!!!!,Red army!!!,maule!!! tikumva kukoma!!!!!,tseketseke!!!!!lyolyolyoooo!!!khatikhati wa mkaka mtima uli zii kulyolyopera!!!
Amene zikumunyasa akazdziponye mu Shire.

Patriotic
Patriotic
9 years ago

Mussa Manyenje mumamunyoza uja siuyu. Timutengatu ife a Silver?

Jeoffrey chimbamba
Jeoffrey chimbamba
9 years ago

Wamkaka kumva kukoma….

aife
aife
9 years ago

That’s what we were expecting after very long time and you know what we have just started next year will be ours that TITTLE.

aife
aife
9 years ago

Koma maule aaaaaaaaaaaaaaaaaaaaa andipangitsa ine kumva kukoma maule omwewo kuti wawawawawawawawa kkkkkkkkkkkkkkkk

Dennis Chipeta
9 years ago

Maule more fire zonse ndizotheka ndi Ambuye palibe wokuyimisani panopa tizingotenga basi zikho zonse!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!

BBsupporter
BBsupporter
9 years ago

Ife ndi akuluakulu enanu mudzitsatira pambuyopo. Makani ana inu Maule woyeee!!!!!

Read previous post:
CounterJab: Mutharika struggling to keep Malawi economy afloat? Karma’s a bitch!

Just six months after sweeping into office in disputed elections, things are not looking up for President Peter Mutharika who...

Close