Email a copy of 'Bullets cut Wanderers' lead to just one point: Malawi TNM Super League ' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
newest oldest most voted
Notify of
mkv
Guest
mkv

Big up maulee

MBWFC
Guest
MBWFC

malamulo akunena kuti mateam onse amane akulimbilana ukatswiri wa ligi amayenela kumamenya magames awo masiku ofanana kuopa match fixing,,kodi kumalawikuno malamulo ake maka inu a solum mumawatenga kuti????

mkv
Guest
mkv

ineso amandidabwisa kwambiri there are full of match fixing these people

Douglas Ndindi
Guest
Douglas Ndindi

With Bullets, it’s not over until it is truly over. It has been said by some wise men that “Bullets n’kumadzulo.” Neighbor should know that ” it is a big mistake to relax when the team breathing down your neck is called Nyasa Big Bullets”. So neighbor ukangoyerekeza kutaya point imodzi, ife Mawule sitilora kuti point imeneyo igwere pansi. Ndithu tiyiwakha isanakhudze nthaka, basi tikatero ndi wautali mpaka tikagwire chikombe cha TNM Super League. Chenjera neighbor, ungadzawone ngati malodza.

Goexy
Guest
Goexy

Kicks of a dying horse.Uku ndikulilira kuusi,Moyale yangokubandurani kumapetopeto ndikuchitaya chikho. Dikirani muliranso simunati, muzifunsa anthu kaye musanapatse timu zina ngati onse ali anu. Peoples timu? zankutu !!

kwacha malawi
Guest
kwacha malawi

Mkodzo FC kulira kumeneku kapena chiyani? Masewera pamafunika wina opambana wina oluza. Osati zankuti ai, chala cha Yehova chikalemba chalemba basi, Neba dikirani madzi adutse uziti ndadala.

mkv
Guest
mkv

ubino wake yinayamba kubandula nomayo fisd yomweyo ndiye si za chilendo thats how mpira ulili man