Email a copy of 'Bullets fail to inspire in 1-1 draw with Red Lions: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets fail to inspire in 1-1 draw with Red Lions: Malawi TNM Super League' to a friend
Raphael Tenthani, fondly known by his peers as R 10, was a revered Malawian journalist who contributed to many news...
THE PROBLEM WITH OUR PLAYERS IS THAT THEY DON’T RESPECT REFEREES’ DECISIONS WHEN THEY THEMSELVES ARE NOT CONVERSANT WITH LAWS OF THE GAME.
Kodi malamulo amagwira ntchito mMalawi? Onani za cashgate, mwinanso malo otengedwa ndi ma foreigners kapena msika wa fodya mMalawi! Tili ndi functional system ngati which we can abide to run our nation for a better Malawi? Ndiye munene za mpira! Onani komwe tikupita – ku chigwembe cha moto. Oh! My God, Malawi akuvayatu uyu inu.
Mwapanga bwino a Bullets, akanakuphani. Amenewo samenya football koma boxing, wrestling, karate……
Still behind.
Muyisova a bullets
ZAWADI CHILUNGA ndi PRINCHARD MWANSA….. ngati ma sports reporter ndi Coach oti wasewerapo mpira ndikhulupirira malamulo ampira mukuwaziwa from A to Z. Player akatukwana Ref, kaya Nzake wa team imodzi or wa team ina or kutukwana supporter amene Lamulo no. 12 likuti chani? Stop kulemba zinthu za ziiii zongopitiliza kusokoneza anthu osaziwa malamulo kupitirirabe kusawadziwa. Zomwe mukunena inuzo kuti he was sent off for protesing referees decision then ikanakhala yellow card ina plus yellow card ina anapatsidwa kale for a reckless tackle it could have made a RED CARD. But the referee flashed a red card directly because the player… Read more »
As Zuma said “take care of your citizes” advising his fellow heads of states,i will also take an advatage to advise SULOM to take care of its referees.To say the truth thy are the referees who struck the violence in super league.
Bb ndi Bb bassi zokoma zikubwera thanks aneba we are behind u watch out