Email a copy of 'Bullets FC eyes K1m first round prize money: Malawi TNM Super League' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets FC eyes K1m first round prize money: Malawi TNM Super League' to a friend
Blantyre based entrepreneur Welkam Phiri and ladies’ top golfer Roza Mbilizi on Saturday emerged the winners for the 2015 Airtel...
Hala BB
Koma maule ndi ulendodi,tiyenawoni anyungwi osawasiya!
BB, zoonadi ndakhulupilira ndi, an predictable. Ma BB omwewo kuti wa wa wa, BB woyeeeeeeeeee.
Wawa maule
Maule omweo kuti waa waa
Mukamva muti bwanjiii! Timuyo timuyo timuyooooo! Inu muziti timu ya fuko!
Zoona maule jst work hard the money is urs, tikamwere zimenezo!!! Enawa akungothandiza amfumu kulezera.
Dont worry guyz this 1million is for you.enawa adikire zipewa zomwe amalandira man of the match zija basi ngati chipukuta misonzi chawo. Maule ndi dilu.
Wina akunva nyunyunyu hahahaha koma neighbour usamalimbane ndi ma Team azibambo.Work Hard Guys mugawane money~yo
Viva mauleeeeer