Email a copy of 'Bullets highly rates Chitowe Stadium standards' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

20 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
?ter cech
8 years ago

koma mbuli zanomazi kulephera kupanga understand cmple english ngati imeneyi zamanyazi go back to xool plz

bryce misomali
8 years ago

maulee amatha guyz

aphiri
aphiri
8 years ago

nzako akachita zabwino kumayamika .

Dennis
8 years ago

Noma ndimakape bullets woyee!

B K C
B K C
8 years ago

I think Munthuwamba has a point, it’s just a matter of praise of the ground for it’s good condition. Big Up Bullets

Mzimba Solola
Mzimba Solola
8 years ago

Mukanakhala kuti mwaluza bwenzi mukuti ku Dwangwa kumatentha, ground silabwino, ref anatikanira penalty hahahah NOMA for life.

zachamba basi
zachamba basi
8 years ago

Makape inu amanoma Ku Zomba munyaso 2-1 Moyale kuwina mauuleeee woyeeeee

Hardson
8 years ago

Kkkkkkkk ndimadabwa kodi mzungumbuzi kaya mbuli akutchulidwa bwanj. Zimene mwachita apa inu mzungu ndi mwano waukuru ndipo Sulom kapena FAM akhoza kukulipitsani! BB ndi timu imene dziko la Malawi ikudalira, powonetsa chitsanzo cha bwino mu legea yayikuru mdziko posagonja mopepera. Apa Bullets monga timu yozindikira ikuyamikira ground kuti chitowe ndi limodzi la ma ground oti ma timu a mdziko muno angamasewererepo mpira.

General Peter
General Peter
8 years ago

@ Trad, Kamuzu Academy might be the best pitch but in this regard we are looking at the grounds where SL teams play. Which team has KA as its home ground? @Mzungumbuli-the name suggests who you really are. Chitowe z home ground 4 Mafco and nt Bulets. Bullets was playing away. @ Alpha-that’s the right understanding and explanation. Stay blessed. @ Vuvuzera-you seem to be speaking same language wt the so called Swazimbuli reporter. @ Sir-Chitowe z really a gud stadium. @ Reporter- Yr gud storyhas been dented by yr failure to explain the real support the company called Illovo… Read more »

Munthuwamba
Munthuwamba
8 years ago

Apa zikuoneka kuti nkhaniyi ena sanaimve bwino. I think chavuta apa ndi chingerezi. Apatu a Bullets akuyamikira a Mafco posankha Chitowe ngati Home Ground limene azisewererapo mpira osati a Bullets asankha Chitowe ngati ground lawo iyayi. Tayambani mwamvetsa nkhani musanaike ma comment.

Read previous post:
Skeffa, Ma Blacks to perform in South Africa

Malawi's leading reggae outfit Black Missionaries alongside Skeffa Chimoto and his Real Sounds band are expected to perform in South...

Close