Email a copy of 'Bullets risk losing Nyasa sponsorship: ‘Civil war’ in Malawi champions camp' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bullets risk losing Nyasa sponsorship: ‘Civil war’ in Malawi champions camp' to a friend
Karonga Central legislator Frank Mwenifumbo on Thursday became the lone voice in parliament welcoming the reduction of Malawi police budget,...
These guyz eeeeeee sakonda team koma yet ndimabige ateam
nthawi ya kondi anthu wake ndi womwewa,lipipa ndianzakewa amamusokoneza kondi.lero ayambanso ife ngati masapota takwiya nawo.
Bullets ndimaikonda bt ma big ake akaona dola mitimayaw sikhala mmalo nde mwina zimawasangala akakhal opanda sponsorship mwin kungowasiy bas
A Bullets alibe mwambo. Tangowasiyani, azitolera ndalama mmaget basi. Asatinyase
Iwe Neba unazolowera kunkhala wopanda wokuthandiza kuba basi mukukangana ziyani?
Neba hehede!!!zamanyazi osakwanaso chaka, mpite kwakhoswe ubachalawu mpakampakatu.Come to Ngokwe more sponsers than ndudu
zikutheka tinaku uza zija zosokoneza zija mesa keep it up fire burn amwali
Bullets ndi-team yachimidz ndipo inazolowera kuvutika komaso ndiyohititsa manyaz ingowasiyan makape aona zochita
Mungonena kuti simunakozeke kuthandiza timu.musachuluse zokamba.
Ukazolowela u bachala ndi choncho. Kupeza mkazi, koma zochita zako kukhalabe ngati bachala. Neba kuzolowela ubachala.