Email a copy of 'Bullets, Wanderers cry foul over gate collections as Sulom institute investigation' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

19 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
nyekhu wa nyekhulani
nyekhu wa nyekhulani
8 years ago

even the name can tell Joka investment? sizodabwisa zimene paja inali homeground ya bb

robert mugawa
robert mugawa
8 years ago

Mudzasiya liti abale kudya nthukuta laazanu

imraan allan
imraan allan
8 years ago

mavuto pa Malawi vuto la zinthu zopanda dongosolo ndi choncho

Bashior
Bashior
8 years ago

Hehede a Malawi tizasintha liti? God will punish you

iwen
iwen
8 years ago

this iz too much!!abale muli ndi msambi.mpaka pamenepo ma player eni ake akuvutika.

Wa Maule weniweni
Wa Maule weniweni
8 years ago

Stadium-gate (kkkk) at its best.

amfana
8 years ago

MUNGOMVA DZINA LAKAMPANIYO JOKA!A? TABESA MAFALANGA TOKHA APA.

ALOSWEA
8 years ago

I am studying estimation ,this is arround thirty million ‘K30million ,ndalama zabendwa arround ‘K15million

mwinimwini wa BB
mwinimwini wa BB
8 years ago

Mbava zimenezi zinalimba ndi Kondi kwambiri last season akuwaletsa kukhala mumagate koma anatembenuza nkhani nkumanena kuti Kondiyo ndi amene akuba chikhalirenicho Kondiyo samakhala pa gate amangolandira zothaitha. mbamvazi zinapeza mwai tsopano poti palibe akuwapinganso ndiyetu basi kuli chipwilikiti kufuna kulemera. zonsezi akutsogolera ndi stone mwamadi, mavuto chiwambo. . ma ticket amapanga print kwa sister wake wa stone , outsource anapanga yawoyawo, kuti azigawana bwino ndalama. opusa kwambiri ndi masapota a bullets amafuna kutsogozedwa ndi mbuli nkumamvera zigawenga ngati zimenezi. zowona mungalore munthu mmodzi akusankhileni executive inu muli ndwiiiii, exedutive ili mkhwapa mwa stone pano. amachita kuwalamula. vuto lina ndi ma… Read more »

Mzimba Solola
Mzimba Solola
8 years ago

BB should be pined to explain, last time Wanderers were the host and managed everything the Derby raised 27 million now BB were the host and raised 16 mllion this is a clear indication that ku Bullets kulibe order when it comes to money. with such behaviours sponsors can not come in to sponsor teams. I strongly believe that ndalama zinabedwa.

Read previous post:
Kasungu market fire damages K10.3bn wealth of goods -Assessment

The Kasungu Municipality assessment committee which comprised of Malawi Police Service, officials from different departments in the municipality and other...

Close