Email a copy of 'Bulllets Vs Wanderers: Malawi Carlsberg Cup final is nigh' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bulllets Vs Wanderers: Malawi Carlsberg Cup final is nigh' to a friend
Mauritius came to the rescue of Athletics Association of Malawi after providing return air tickets to enable the association athlete...
Eeeeh tionane mawaaa ilikoooo
maule 4 life
BB 4 life
GUYZ MWINA TANTHAUZO LA NOMA CIMUKULIZIWA NALI: NO=PALIBE; MA=SHRT OF MONEY WHCH Z NO MONEY FOR NYELERE.MAULE ND MAULE SIZE YATHU ND FOMBON FC. MANOMA+BANKERS= MAULE ANA MWACHEPA INU! KKKKK!
Viva Nomads
Sunday pa Civil Stadium pali chaka cha makhwangwala kuzatola mapale onse atabandulidwa ndi nyerere zaukali zedi. Manoma woye. Nathundu woye. Jini Chalungama ku Ntchisi ziiiii!!!!!!! koma mapare ulendo wobwerera kwanu uzalemera zedi. Ndipo muzayenda ndi usiku basi mutamusiya mwana wanu komweko ife nyerere mkumutenga.
So God hel us ( manoma) to defeat mapare in the All Mighty Name of JESUS. Amen.
sunday pa sivo stedium pali msonkhano wa akhwangwala azakhala akutola nyerere zoola z omwe ife tizaphe loweluka.
So God help us (BIG BULLETS FC), in the mighty name of JESUS
MPIRA NDI 90 MIN NOMA WOYEE