Email a copy of 'Bunda Filling Station to fuel development at LUANAR' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bunda Filling Station to fuel development at LUANAR' to a friend
Football Association of Malawi (FAM) has assured Super League clubs and soccer loving Malawians that the country's top flight will...
Thumps up LUNAR. Chancellor College and Malawi Polytechnic should also come up with businesses / companies. Don’t just wait for govt subvention / funding. The world is changing and you need to change also.
Univesity ndiye imeneyi osati zinazi.
SEYANI UYU NDI WA MULHAKO IJA ETI?????
Whats wrong with being Mlomwe? Wakutuma ndi ndani mbuzi iwe
Koma akadakhala wa mtundu wanu? Tisayang’ane za mtundu
koma zomuyeneretsa munthu pa udindo wache. Boma
lidasankha professor seyani kukhala mkulu wa Luanar
Council chifukwa cha ukaswiri wache wa za malimidwe,
za chilengedwe, zakafukufuku komanso maphunziro ache mwa
zina. Mzathuyi adakaphunzira ku Chanco, Bunda, Reading
University mpaka kukatsilizira ku Oxford University. Komanso
wagwira ntchito muno m’Malawi ndi ku Ulaya. Palibe za uLhomwe
apa koma u kadolo. Inu a Vipers za chamba ai, samalirani.