Email a copy of 'Buyer shot dead over K200, 000: Malawi Police intensify investigations' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Buyer shot dead over K200, 000: Malawi Police intensify investigations' to a friend
Malawi High Court has ruled that 11 prostitutes who were forced to take HIV tests by police six years ago...
Akuba inu mverani kuba muleke mukapitiza muona polekera.
Pliz police shoot to kill is the best policy for Malawi . If NGOs and court are disturbing you , do not we shall deal
Zikunyansani bwanji ena a police akugwidwa kuphananso nokha
Nkhanza ndi umbanda siyani tsiku la 40 lizakukwanilani
GIVE US OUR OWN SECURITY IN OUR NEIGHBORHOOD MR PRESIDENT
ZIGANDANGA INU, KODI MUNAKHALA BWANJI?KUM’BERA MUNTHU KOMANSO KUMUPHA.SATANA WAMKULU.SINTHANI,FUNANI NJIRA ZINA ZA BWINO ZOFUNIRA NDALAMA.
anthu muziyankhula bwino zilizonse mumangoti apolisi akuba nawo, ife tidzakusiirani ntchito muzakhale ndi bata mmalawi muno, ife apolisi zimatinyasa kwambiri
Abale mpaka munthu kumupha chifukwa cha k200,000 basi komanso munthuyo siyake so sad RIP
Ubututu basi
Mfufuzeni Supervisor. He deliberately gave the guy the money in the presence of people to show off komanso atha kukhalanso yemweyo we have people who could give you money and later send thugs to rob you of the same money. Cholinga chopelekera pagulu amafuna kuti ndalamayo ma thugs akakayitenganso, mnzake adzalephere kunena kuti waberedwa amafuna gululo lizizaikira umboni kuti analandiradi ndalama mnzakeyo. Stupid supervisor waphetsa mnzako.