Email a copy of 'BWB disconnects water at Malawi govt offices over unpaid K2.6m bill' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'BWB disconnects water at Malawi govt offices over unpaid K2.6m bill' to a friend
The First Lady Professor Gertrude Mutharika, through the Beautify Malawi Trust (BEAM) on Tuesday handed over medical equipment worth K90...
Kodi savings ya ma MP ija singapite kumeneku?
Kabweranitu ticheze apa, iyitu si M.C.P. koma D.P.P Government, umbuli basi…………………………………………..
BWANA CHAWEZA MUTITSEGULIRE MADZI INU NDI BOMA IFENSO NDI BOMA
MA FUNDING AKUMAKHALA OCHEPA NANGA REGIONAL INFORMATION OFFICE ONE MILLION YOMWEYO ALIPIRIRE MADZI YOWEYO MAGETSI YOMWEYO AGULE MAFUTA YOMWEYO AYENDETSERE OFESI IGWIRA? BOMA MUONJEZERE NDALAMA KUMA DEPARTMENT
Bwana Chaweza mwayamba ndi Phumatu. ino ndi BWB kunali anzanu aphuma choncho muwafunse kuti pano ali kuti ?
Kuno Ku Regional Water Office anatiduliraso. If BWB can disconnect its parent ministry what more ndi enanu