Email a copy of 'Call logs in Mphwiyo’s case suspected to be doctored -Wapona' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Call logs in Mphwiyo’s case suspected to be doctored -Wapona' to a friend
Be Forward Wanderers coach Elia Kananji says the Easter friendly games against Civo United and Mafco in Lilongwe have assisted...
Mukutisuzga waka apa. Nothing will come out of this.
History tells me that government hired incompetent lawyers and lacks preparation that leads them to loss most cases. It is clear this case the govt has lost. We expect to pay huge sum money to the accused. Anything can be doctored including call log. Comments reveal the ignorance of some Nyasas on the art of doctoring. Koma umbuli ndi matendadi kwambiri akwatu ku south ndi anzatu a pakati.
Mafia style the one with more money will win the case
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk!! kuyesetsa kupeza tinjira topulumukira… uuuuuuuuuuuuuhhh! sindikupaona ine, poti nkunamira tu defence team woyeeeeeeee! asakugwetseni mphwayi mbala zophunzira zachabechabe, zinaononga dziko lanthu la Mkaka ndi uchi, kuzerezetsa achikulire, achina Atcheya, Bingu , Kassim chilumpha, kumazunzitsa mabanja awo awo aku mwa wa mkaka…..lero la 40 lakwana..! wihiiii! mwina dziko nkukonzeka. Mbava ya lawyer yayikulu yikagwida, mwina azinzake nkubweza magiya. Rachel Kachale more fireeeee!
Kita if they logs were doctored bweretsa ako tipange share notes…….umbuli ophunzira nao . Atumbuka osukusula kuukulu akhakhakha a dyabulosi a dyabulosi a dyabulosi a thakati inu
nde chiyani
Comment zankutu!
Alungwana you are talking. Anthuwa kaya ndi chiyani kuchedwetsa kumeneku nzake ali pa business koma enawa sakudziwa. Kaya! Misonkho ya a Malawi izingopita mmadzi za ziii.
Call logs can not be doctored . Aitel musainamizire . Sovani
Wapona ndi Kasambala one side?Awina kale mlanduwu!! Kikiki