Email a copy of 'Callista sues Jeffrey for K500m defamation suit on Bingu death' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Callista sues Jeffrey for K500m defamation suit on Bingu death' to a friend
Defiant ruling top Democratic Progressive Party (DPP) officials made disparaging remarks against former First Lady Callista Mutharika and Patricia Kaliati...
Chipani chosowa chochita chimatchula anthu akufa. Let Bingu rest in peace, he developed this nations unlike the failures we are seeing. Callista we are behind you, I love you, will you marry me?
Callista koma nde mwagwila chipwisitu game yagona zoima wakanatu uyu mmati muli pa mbuyo pakeyu koma wakuputsitsani pepani mama zimachitika
Nanunso inu kuchititsa manyazi……………..! Anthuwa amafuna Chilima adzakhale president wa dziko osati chipani chikha! Bwanji ngati simumamva chizungu osafunsa kaye kwa ena kuti mumvetsetse zimene Chilima wanena bwanji? Chilima said he will come back in due course to give his response on whether he will contest as a presidential candidate or not? Ndiye ukati game yagona zoima wakana, wakana chani? Ndipo iweyo zokanazo wazitenga kwa ndani? Pa zomwe walankhula wanenapo zokana? Chilima wanena kuti sapikisana nawo pa mpando wa presidential candidate for DPP ndipo chipani cha DPP wachituluka…………………………….!! Nanga zimenezi zikutanthauza kuti wati sadzapikisana nawo pa mpando wa u president… Read more »
let the truth prevail….. justice rather than mercy
A Jeffrey amati ukakwera pa msana wa njonvu usamati kulibe mame, moti ndizoona zomwe munalankhulazo. U were so over joyous
Iam suing Calisita 500millionn kwacha and one tambala
Koma Galu uyu amaifunadi ndata farm. So you call it a movement. How much will they get if allowed to be in power. Wopusa ndi Ncilima.
Don’t bring your personal issues here………………………………………..!! Mukungoonetsa kepepela komanso uchitsiru wanu!! Za Ndatazo ngati mukulimbilirana ndi ku Thyolo komweko!! After all belonging to one family does not mean all family members should not be disagreeing in political matters!! Kodi sukulu munalekeza chani? You sound so brain washed…………………………………………………!! Mxiiiiiiiiiiii
Iam also ready to sue Calisita for calling Peter an old Man. That’s being disrespectful to elderly people people.
500 million I have never heard. Ncilima you want this money to run your campaign. Galu Calisita wagwa
Nayo
Ok, on her behalf sincerely receive my apologies for calling him old, from today, let us be calling him a youth or a teenager!!
Abale why should that be a mistake, when the same team is calling others babies to lead Malawi? Mwakuti ma babies nawonso akwiye chifukwa atchulidwa ma baby?? Kodi moti siyikhalanso nhkani enafe tikanena kuti Peter ndi kamwana kakang’ono ng’ono!! Ndimayesa chimenecho ndi chimene chimafunika kukhala chipongweeeeeeeeeeee? Koma ili gulu limamva zozondoka ndithudiiiiiiiiiiii Pitani ku COMESA mukagule juvenile hormone basi, mwina akhoza kubwelera mu zaka………………….!
Callista is a stupid woman. Wagwa nayo. Wapysa alibe ndalama.
Way to go Callista. Osamusiya ameyo achenjere. Amadziyesa kuti ndikatswiri.
She is part of the entire game so is Jeffrey. Both are politicians of inadequate temperament there is no cause for going to court. The nation is fortunate in that Callista has dismally failed the test she can’t lead the nation all citizens with loud mouth will end up in courts a simple verbal scratch will spark a chain of legal repercussions. She will be unleashing her legal hounds a politician with leadership qualities only squirms when the balls are squeezed. Hurray Callista will get the monies not any leadership of substance within Malawi. She won’t dazzle anyone with her… Read more »
Mwachepetsa Mami. Mukanangomatchisa ndi K70bn afuna iye ija. That was defamatory of the century and she must pay for that
Jeffery will sleep around and raise this money.